Thu Oct 07 2021 14:15:56 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:15:57 +02:00
parent e139a6d845
commit ff62311d9a
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
08/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Mkazi wolankhula yekha ndinali khoma, ndipo mabere anga anali ngati nsanja zazitali; choncho ndili m'maso mwake ngati wobweretsa mtendere. Mkazi kuyankhula yekha

1
08/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Solomo anali ndi munda wamphesa ku Baal Hamon. Anapereka mundawo kwa iwo amene adzausamalira. Aliyense anayenera kubweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000. \v 12 Munda wanga wamphesa, wanga womwe, uli pamaso panga; masekeli chikwi chimodzi ndi anu, Solomo, ndipo masekeli mazana awiriwo ndi a osunga zipatso zake.

1
08/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Mwamuna amene akuyankhula ndi mkazi Inu amene mumakhala m'minda, anzanga akumvera mawu anu; ndisiyeni ndimve.

1
08/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo Fulumira, wokondedwa wanga, ndipo khala ngati mphoyo kapena mwana wa mbawala pamapiri a zonunkhira.

View File

@ -118,6 +118,10 @@
"08-06",
"08-07",
"08-08",
"08-09"
"08-09",
"08-10",
"08-11",
"08-13",
"08-14"
]
}