Thu Oct 07 2021 14:14:23 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:14:23 +02:00
parent 873b2085cb
commit e139a6d845
6 changed files with 11 additions and 1 deletions

1
08/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Akazi aku Yerusalemu akuyankhula 5Ndani amene akubwera kuchokera kuchipululu, kutsamira wokondedwa wake? Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo ndinakudzutsa pamenepo mai ako adakudyetsa; komweko adakubalira, nakubala.

1
08/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Ndiike pamtima pako ngati chisindikizo, ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi nchamphamvu ngati imfa. Kudzipereka kosalamulirika kuli kosalekeza monga Manda; malawi ake anaphulika; ndi lawi lamoto, lawi loyaka moto koposa moto wina uliwonse.

1
08/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Madzi othamanga sangathe kuzimitsa chikondi, ngakhale kusefukira kwamadzi sikungakusunthire. Ngati munthu atapereka zonse zomwe zili mnyumba mwake mwachikondi, mwayiwo unganyozedwe konse.

1
08/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Abale a mkaziyo amalankhulana pakati pawo Tili ndi mlongo wathu wamng'ono, ndipo mabere ake sanakulebe. Kodi tingatani kwa mlongo wathu patsiku lomwe adzalonjezedwe kukwatiwa?

1
08/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Akakhala khoma, tim'mangira nsanja yasiliva. Ngati ali khomo, timukongoletsa ndi matabwa amkungudza.

View File

@ -113,6 +113,11 @@
"08-title",
"08-01",
"08-02",
"08-04"
"08-04",
"08-05",
"08-06",
"08-07",
"08-08",
"08-09"
]
}