diff --git a/08/05.txt b/08/05.txt new file mode 100644 index 0000000..63daf85 --- /dev/null +++ b/08/05.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 5 Akazi aku Yerusalemu akuyankhula 5Ndani amene akubwera kuchokera kuchipululu, kutsamira wokondedwa wake? Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo ndinakudzutsa pamenepo mai ako adakudyetsa; komweko adakubalira, nakubala. \ No newline at end of file diff --git a/08/06.txt b/08/06.txt new file mode 100644 index 0000000..5c7dc88 --- /dev/null +++ b/08/06.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 6 Ndiike pamtima pako ngati chisindikizo, ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi nchamphamvu ngati imfa. Kudzipereka kosalamulirika kuli kosalekeza monga Manda; malawi ake anaphulika; ndi lawi lamoto, lawi loyaka moto koposa moto wina uliwonse. \ No newline at end of file diff --git a/08/07.txt b/08/07.txt new file mode 100644 index 0000000..1e7c493 --- /dev/null +++ b/08/07.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 7 Madzi othamanga sangathe kuzimitsa chikondi, ngakhale kusefukira kwamadzi sikungakusunthire. Ngati munthu atapereka zonse zomwe zili mnyumba mwake mwachikondi, mwayiwo unganyozedwe konse. \ No newline at end of file diff --git a/08/08.txt b/08/08.txt new file mode 100644 index 0000000..1435bac --- /dev/null +++ b/08/08.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 8 Abale a mkaziyo amalankhulana pakati pawo Tili ndi mlongo wathu wamng'ono, ndipo mabere ake sanakulebe. Kodi tingatani kwa mlongo wathu patsiku lomwe adzalonjezedwe kukwatiwa? \ No newline at end of file diff --git a/08/09.txt b/08/09.txt new file mode 100644 index 0000000..43211bf --- /dev/null +++ b/08/09.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 9 Akakhala khoma, tim'mangira nsanja yasiliva. Ngati ali khomo, timukongoletsa ndi matabwa amkungudza. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 92733c1..21005e0 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -113,6 +113,11 @@ "08-title", "08-01", "08-02", - "08-04" + "08-04", + "08-05", + "08-06", + "08-07", + "08-08", + "08-09" ] } \ No newline at end of file