Thu Oct 07 2021 14:12:22 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:12:23 +02:00
parent 512c0ee00f
commit 873b2085cb
4 changed files with 7 additions and 1 deletions

1
08/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 8 \v 1 Ndikulakalaka ukadakhala ngati mchimwene wanga, amene adayamwa mabere a amayi anga. Nthawi zonse ndikakumana nanu panja, ndimakhoza kukupsopsona, ndipo palibe amene amandinyoza.

1
08/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Ndikanakutsogolera ndi kukulowetsa m'nyumba ya mayi anga, amene anali kundiphunzitsa. Ndikadakumwetsa vinyo wokometsera ndi zakumwa za makangaza anga. Mayiyo akuyankhula yekha \v 3 Dzanja lake lamanzere lili kumutu kwanga ndipo dzanja lake lamanja landikumbatira.

1
08/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Mkazi amene akuyankhula ndi akazi ena ndikufuna ndikulumbireni, ana aakazi a ku Yerusalemu, kuti simudzadzutsa kapena kudzutsa chikondi kufikira chikadzafuna.

View File

@ -110,6 +110,9 @@
"07-10",
"07-12",
"07-13",
"08-title"
"08-title",
"08-01",
"08-02",
"08-04"
]
}