diff --git a/08/01.txt b/08/01.txt new file mode 100644 index 0000000..b6ff9dc --- /dev/null +++ b/08/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 8 \v 1 Ndikulakalaka ukadakhala ngati mchimwene wanga, amene adayamwa mabere a amayi anga. Nthawi zonse ndikakumana nanu panja, ndimakhoza kukupsopsona, ndipo palibe amene amandinyoza. \ No newline at end of file diff --git a/08/02.txt b/08/02.txt new file mode 100644 index 0000000..6e39636 --- /dev/null +++ b/08/02.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 2 Ndikanakutsogolera ndi kukulowetsa m'nyumba ya mayi anga, amene anali kundiphunzitsa. Ndikadakumwetsa vinyo wokometsera ndi zakumwa za makangaza anga. Mayiyo akuyankhula yekha \v 3 Dzanja lake lamanzere lili kumutu kwanga ndipo dzanja lake lamanja landikumbatira. \ No newline at end of file diff --git a/08/04.txt b/08/04.txt new file mode 100644 index 0000000..430383e --- /dev/null +++ b/08/04.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 4 Mkazi amene akuyankhula ndi akazi ena ndikufuna ndikulumbireni, ana aakazi a ku Yerusalemu, kuti simudzadzutsa kapena kudzutsa chikondi kufikira chikadzafuna. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 8d0c460..92733c1 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -110,6 +110,9 @@ "07-10", "07-12", "07-13", - "08-title" + "08-title", + "08-01", + "08-02", + "08-04" ] } \ No newline at end of file