diff --git a/08/10.txt b/08/10.txt new file mode 100644 index 0000000..ac674ef --- /dev/null +++ b/08/10.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 10 Mkazi wolankhula yekha ndinali khoma, ndipo mabere anga anali ngati nsanja zazitali; choncho ndili m'maso mwake ngati wobweretsa mtendere. Mkazi kuyankhula yekha \ No newline at end of file diff --git a/08/11.txt b/08/11.txt new file mode 100644 index 0000000..0bd1159 --- /dev/null +++ b/08/11.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 11 Solomo anali ndi munda wamphesa ku Baal Hamon. Anapereka mundawo kwa iwo amene adzausamalira. Aliyense anayenera kubweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000. \v 12 Munda wanga wamphesa, wanga womwe, uli pamaso panga; masekeli chikwi chimodzi ndi anu, Solomo, ndipo masekeli mazana awiriwo ndi a osunga zipatso zake. \ No newline at end of file diff --git a/08/13.txt b/08/13.txt new file mode 100644 index 0000000..7010ea1 --- /dev/null +++ b/08/13.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 13 Mwamuna amene akuyankhula ndi mkazi Inu amene mumakhala m'minda, anzanga akumvera mawu anu; ndisiyeni ndimve. \ No newline at end of file diff --git a/08/14.txt b/08/14.txt new file mode 100644 index 0000000..ed1b70c --- /dev/null +++ b/08/14.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 14 Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo Fulumira, wokondedwa wanga, ndipo khala ngati mphoyo kapena mwana wa mbawala pamapiri a zonunkhira. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 21005e0..8b985cf 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -118,6 +118,10 @@ "08-06", "08-07", "08-08", - "08-09" + "08-09", + "08-10", + "08-11", + "08-13", + "08-14" ] } \ No newline at end of file