Thu Jan 02 2020 18:50:41 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2020-01-02 18:50:42 +02:00
parent 8d56d90fc9
commit 88f15ecbb9
12 changed files with 25 additions and 11 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 6 \v 7 Ninaona mwana wa nkhosa kuimilira pakati pa mpando wa chimfumu na zamoyo zinai ndinso pakati pa akulu 24. Anaoneka monga anali ataphedwa. Anali na manyanga 7 na menso 7; Aya ni mizimu 7 ya Mulungu yotumizidwa ku dziko lonse lapansi. Anapita ndi kukatenga buku lija ku dzanja la manja la yemwe akhala pa mpando wa chimfumu.
\v 6 Ninaona mwana wa nkhosa kuimilira pakati pa mpando wa chimfumu na zamoyo zinai ndinso pakati pa akulu 24. Anaoneka monga anali ataphedwa. Anali na manyanga 7 na menso 7; Aya ni mizimu 7 ya Mulungu yotumizidwa ku dziko lonse lapansi. \v 7 Anapita ndi kukatenga buku lija ku dzanja la manja la yemwe akhala pa mpando wa chimfumu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 \v 10 Anaimba nyimbo ya sopano: Ndinu oyenera kutenga buku ndi kulisegula zosindikizira zake. Chifukwa munaphedwa, ndipo na magazi anu munagula anthu a mitundu yonse kwa atate, chilankhulo, mtundu, anthu na maiko. Munawapanga ufumu, ndi ansembe kutumikira Mulungu wathu, ndipo azakhala pa dziko la pansi."
\v 9 Anaimba nyimbo ya sopano: Ndinu oyenera kutenga buku ndi kulisegula zosindikizira zake. Chifukwa munaphedwa, ndipo na magazi anu munagula anthu a mitundu yonse kwa atate, chilankhulo, mtundu, anthu na maiko. \v 10 Munawapanga ufumu, ndi ansembe kutumikira Mulungu wathu, ndipo azakhala pa dziko la pansi."

View File

@ -1 +1 @@
\v 11 \v 12 Ndipo ninaona ndi kumva mau ya angelo ambiri kuzungulira mpando wa chimfumu, zamoyo zinai ndi akulu 24. Unyinji wao unali zikwi ndi zikwi. Ananena mu mau okweza, "Ndi oyenera mwana wa nkhosa yemwe anaphedwa kulandira mphamvu, ulemelero,nzeru, ulemu na matamando."
\v 11 Ndipo ninaona ndi kumva mau ya angelo ambiri kuzungulira mpando wa chimfumu, zamoyo zinai ndi akulu 24. Unyinji wao unali zikwi ndi zikwi. \v 12 Ananena mu mau okweza, "Ndi oyenera mwana wa nkhosa yemwe anaphedwa kulandira mphamvu, ulemelero,nzeru, ulemu na matamando."

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 Ninamva cholengedwa chilichonse kumwamba, padziko la pansi, na pansi pa dziko la pansi ni mu manzi- zonse zopezekamo- kukamba ati, "kwa iye okhala pa mpando wa chimfumu na kwa mwana wa nkhosa, kukhale matamando, ulemu, ulemelero ndi mphamvu zolamulira nthawi zonse." Zamoyo zinai zinati, "Amen!" ndipo akulu anazigwesa pansi ndi kulambira.
\v 13 Ninamva cholengedwa chilichonse kumwamba, padziko la pansi, na pansi pa dziko la pansi ni mu manzi- zonse zopezekamo- kukamba ati, "kwa iye okhala pa mpando wa chimfumu na kwa mwana wa nkhosa, kukhale matamando, ulemu, ulemelero ndi mphamvu zolamulira nthawi zonse." \v 14 Zamoyo zinai zinati, "Amen!" ndipo akulu anazigwesa pansi ndi kulambira.

View File

@ -1 +1 @@
\c 6 \v 1 \v 2 Ninaona pamene mwana wa nkhosa anasegula imozi mwa zosindikizira 7, ndipo ninamva cimozi mwa zamoyo zinai zija kukamba kuti mu mau amene anamveka monga mabingu, "Bwera!" Ninaona ndipo panali kavalo oyera. Okwerapo ananyamula uta, ndipo anapasiwa kolona. Anachoka ngati opambana kuti apambane.
\c 6 \v 1 Ninaona pamene mwana wa nkhosa anasegula imozi mwa zosindikizira 7, ndipo ninamva cimozi mwa zamoyo zinai zija kukamba kuti mu mau amene anamveka monga mabingu, "Bwera!" \v 2 Ninaona ndipo panali kavalo oyera. Okwerapo ananyamula uta, ndipo anapasiwa kolona. Anachoka ngati opambana kuti apambane.

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, kuti anthu aphane okha-okha. Okwerapo ameneyu anapasidwa chimpeni chachikulu.
\v 3 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" \v 4 Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, kuti anthu aphane okha-okha. Okwerapo ameneyu anapasidwa chimpeni chachikulu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 \v 6 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa dinari imozi. Koma osaononga mafuta na vinyo."
\v 5 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. \v 6 Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa dinari imozi. Koma osaononga mafuta na vinyo."

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 4, ninamvera mau ya chamoyo cha chinai kukamba ati, "bwera!" ndipo ninaona kavalo ombuwilira. Ndipo okwerapo dzina lake ni imfa, ndipo hade anali kulondola kumbuyo. Anapasidwa mphamvu ya gawo la dziko, kupha na chimpeni, njala na matenda na nyama za musanga za padziko.
\v 7 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 4, ninamvera mau ya chamoyo cha chinai kukamba ati, "bwera!" \v 8 ndipo ninaona kavalo ombuwilira. Ndipo okwerapo dzina lake ni imfa, ndipo hade anali kulondola kumbuyo. Anapasidwa mphamvu ya gawo la dziko, kupha na chimpeni, njala na matenda na nyama za musanga za padziko.

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha namba 5, ninaona pansi pa guwa mizimu ya aja omwe anaphedwa chifukwa cha mau a Mulungu na umboni omwe anali nao. Analira na mau okweza, "Mpaka liti, olamulira onse, oyera ndi wachoonadi, pomwe muzaweruza omwe ankhala pa dziko la pansi, pomwe muzabwezera magazi athu?" Ndipo aliyense wa iwo anapasidwa mkanjo oyera, ndipo anauzidwa kuti ayembekeze pang'ono mpaka nambala ya akapolo anzao na bale ao ikwane omwe ayenera kuphedwa, monga momwe iwo anaphedwa.
\v 9 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha namba 5, ninaona pansi pa guwa mizimu ya aja omwe anaphedwa chifukwa cha mau a Mulungu na umboni omwe anali nao. \v 10 Analira na mau okweza, "Mpaka liti, olamulira onse, oyera ndi wachoonadi, pomwe muzaweruza omwe ankhala pa dziko la pansi, pomwe muzabwezera magazi athu?" \v 11 Ndipo aliyense wa iwo anapasidwa mkanjo oyera, ndipo anauzidwa kuti ayembekeze pang'ono mpaka nambala ya akapolo anzao na bale ao ikwane omwe ayenera kuphedwa, monga momwe iwo anaphedwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 12 \v 13 \v 14 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 6, ninaona ndipo panali chibvomezi champhamvu. Dzuwa inada monga chovala chakutha ndipo mwezi unakhala monga magazi. Nyenyezi za kumwamba zinagwa pansi, monga mwamene mtengo wa mkuyu umagwesera zipaso zake zosapya ngati mphepo yakuntha. Kumwamba kunasoba monga buku lamene alupeteka. Mapiri na zitunda zinachosedwa pa malo ake.
\v 12 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 6, ninaona ndipo panali chibvomezi champhamvu. Dzuwa inada monga chovala chakutha ndipo mwezi unakhala monga magazi. \v 13 Nyenyezi za kumwamba zinagwa pansi, monga mwamene mtengo wa mkuyu umagwesera zipaso zake zosapya ngati mphepo yakuntha. \v 14 Kumwamba kunasoba monga buku lamene alupeteka. Mapiri na zitunda zinachosedwa pa malo ake.

View File

@ -1 +1 @@
\v 15 \v 16 \v 17 Ndipo mamfumu na anthu olemekezeka, akulu a asilikali, olemera, amphamvu, ena onse, omasuka ni akapolo, anabisala mu mphanga na mu minyala ya m'mapiri. Ananena kwa miyala na mapiri, "Tigweleni!" tibiseni ku nkhope ya iye amene ali pa mpando wa chimfumu ni ku mkwiyo wa mwana wa nkhosa. Chifukwa siku la mphamvu la mkwiyo wao lafika. Ndani azakwanisa kuimilira?"
\v 15 Ndipo mamfumu na anthu olemekezeka, akulu a asilikali, olemera, amphamvu, ena onse, omasuka ni akapolo, anabisala mu mphanga na mu minyala ya m'mapiri. \v 16 Ananena kwa miyala na mapiri, "Tigweleni!" tibiseni ku nkhope ya iye amene ali pa mpando wa chimfumu ni ku mkwiyo wa mwana wa nkhosa. \v 17 Chifukwa siku la mphamvu la mkwiyo wao lafika. Ndani azakwanisa kuimilira?"

View File

@ -84,6 +84,20 @@
"05-title",
"05-01",
"05-03",
"05-06",
"05-08",
"05-09",
"05-11",
"05-13",
"06-title",
"06-01",
"06-03",
"06-05",
"06-07",
"06-09",
"06-12",
"06-15",
"07-title",
"10-01",
"10-03",
"10-05",