Thu Jan 02 2020 18:48:41 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2020-01-02 18:48:42 +02:00
parent 3b24623e76
commit 8d56d90fc9
9 changed files with 19 additions and 8 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 \v 20 Nimazuzula aliyense wamene nikonda, ni kuwauza mwamene ayenera kunkhalira. Kotero, cita changu na kutembenuka. Onani! naima pa khomo nigogoda. Ngati wina amvera mau anga na kusegulako, nizaloba mnyumba yake nakudya nayeve, yeve na ine.
\v 19 Nimazuzula aliyense wamene nikonda, ni kuwauza mwamene ayenera kunkhalira. Kotero, cita changu na kutembenuka. \v 20 Onani! naima pa khomo nigogoda. Ngati wina amvera mau anga na kusegulako, nizaloba mnyumba yake nakudya nayeve, yeve na ine.

View File

@ -1 +1 @@
\v 21 \v 22 Wamene apambana, nizamupasa mwai onkhala na ine pa mpando wa chimfumu, mwamene ine ninapambana na kunkhala na atate pa mpando wa chimfumu. Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba kwa mipingo.
\v 21 Wamene apambana, nizamupasa mwai onkhala na ine pa mpando wa chimfumu, mwamene ine ninapambana na kunkhala na atate pa mpando wa chimfumu. \v 22 Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba kwa mipingo.

View File

@ -1 +1 @@
\c 4 \v 1 \v 2 \v 3 Pambuyo pa izi zinthu ninayang'ana, ndipo ninaona chiseko choseguka kumwamba. Mau oyamba omwe ninamva omwe yamakamba na ine monga lipenga kukamba ati, "bwera kuno, ndipo nizakuuza zamene zizachitika pambuyo pa izi." Pa nthawi imeneyi ninali mu mzimu, ndipo ninaona kunali mpando wa chimfumu ku mwamba, ndipo panali wina onkhalapo. Wamene analipo amaoneka monga jasper na carnelian. Panali utawaleza kuzungulira pa mpando wa mfumu. Utawaleza unaoneka umaoneka monga mwala wa emerald.
\c 4 \v 1 Pambuyo pa izi zinthu ninayang'ana, ndipo ninaona chiseko choseguka kumwamba. Mau oyamba omwe ninamva omwe yamakamba na ine monga lipenga kukamba ati, "bwera kuno, ndipo nizakuuza zamene zizachitika pambuyo pa izi." \v 2 Pa nthawi imeneyi ninali mu mzimu, ndipo ninaona kunali mpando wa chimfumu ku mwamba, ndipo panali wina onkhalapo. \v 3 Wamene analipo amaoneka monga jasper na carnelian. Panali utawaleza kuzungulira pa mpando wa mfumu. Utawaleza unaoneka umaoneka monga mwala wa emerald.

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 5 Kuzugulira mpando panaliso mipando 24, ndipo amene anankhala pa mipando imeneyi ni banthu bakulu-bakulu, obvala zobavala zoyera, na ma kolona ya golide ku mutu yao. Pa mpando wa chimfumu panachoka moto wa kaleza, kugunda na kung'anima kwa mphenzi. Nyale 7 zimayaka pasogolo pa mpando, nyale zomwe ni mizimu 7 ya Mulungu.
\v 4 Kuzugulira mpando panaliso mipando 24, ndipo amene anankhala pa mipando imeneyi ni banthu bakulu-bakulu, obvala zobavala zoyera, na ma kolona ya golide ku mutu yao. \v 5 Pa mpando wa chimfumu panachoka moto wa kaleza, kugunda na kung'anima kwa mphenzi. Nyale 7 zimayaka pasogolo pa mpando, nyale zomwe ni mizimu 7 ya Mulungu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 Chamoyo choyamba chenze kuoneka monga nkhalamu, cha chiwiri chenze kuoneka monga mwana wa ng'ombe, cha chitatu monga pa menso pa munthu, ndipo cha namba 4 chinali kuoneka monga mbalani youluka. Zamoyo zimenez chilichonse chinali na mapiko 6, yozula menso pansi na pamwamba. Usiku na muzuba sivileka kukamba ati, "Oyera, Oyera, Oyera ni Mulungu wa mphamvu zonse amene analiko, aliko, ndipo azankhalako."
\v 7 Chamoyo choyamba chenze kuoneka monga nkhalamu, cha chiwiri chenze kuoneka monga mwana wa ng'ombe, cha chitatu monga pa menso pa munthu, ndipo cha namba 4 chinali kuoneka monga mbalani youluka. \v 8 Zamoyo zimenez chilichonse chinali na mapiko 6, yozula menso pansi na pamwamba. Usiku na muzuba sivileka kukamba ati, "Oyera, Oyera, Oyera ni Mulungu wa mphamvu zonse amene analiko, aliko, ndipo azankhalako."

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Nthawi zonse pamene za moyo zipereka ulemelero, ulemu na matamando kwa amene ankhala pa mpando wa chimfumu, wamene ankhala kwa muyaya, akulu 24 amazigwesa pansi kulambira iye amene ankhala pa mpando wa chimfumu. Bamagwada kwa iye amene ankhala muyaya, ndipo amaponya pansi ma kolona yao ku mpando, kukamba kuti, "Ndinu oyenera, ambuye athu na Mulungu wathu, kulandira ulemu, ulemelero ndi mphamvu. Chifukwa munalenga zinthu zonse, ndipo mwa chifuniro chanu, zinankhalako ndipo zinalengewa."
\v 9 Nthawi zonse pamene za moyo zipereka ulemelero, ulemu na matamando kwa amene ankhala pa mpando wa chimfumu, wamene ankhala kwa muyaya, \v 10 akulu 24 amazigwesa pansi kulambira iye amene ankhala pa mpando wa chimfumu. Bamagwada kwa iye amene ankhala muyaya, ndipo amaponya pansi ma kolona yao ku mpando, kukamba kuti, \v 11 "Ndinu oyenera, ambuye athu na Mulungu wathu, kulandira ulemu, ulemelero ndi mphamvu. Chifukwa munalenga zinthu zonse, ndipo mwa chifuniro chanu, zinankhalako ndipo zinalengewa."

View File

@ -1 +1 @@
\c 5 \v 1 \v 2 Ndipo ninaona mumanja mwa iye amene anakhala pa mpando wa chimfumu ku dzanja la manja lake, chi buku cholembewa mbali zonse ziwiri. Inali yosindikiziwa na zosindikizira 7. Ninaona mngelo wa mphamvu kukuwa ni mau okweza, "Ndani oyenera kusegula buku na zosindikizira zake?"
\c 5 \v 1 Ndipo ninaona mumanja mwa iye amene anakhala pa mpando wa chimfumu ku dzanja la manja lake, chi buku cholembewa mbali zonse ziwiri. Inali yosindikiziwa na zosindikizira 7. \v 2 Ninaona mngelo wa mphamvu kukuwa ni mau okweza, "Ndani oyenera kusegula buku na zosindikizira zake?"

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Palibe aliyense kumwamba, padziko la pansi kapena pansi pa dziko yemwe anali oyenera kusegula buku kapena kuwerenga. Ninalira maningi chifukwa panalibe aliyense oyenera kusegula kapena kuwerenga buku. Koma m'mozi wa akulu-akulu anati kwa ine, "Usalire. Ona! nkhalamu ya mtundu wa ayuda, muzu wa Davide, wapambana. Akwanisa kusegula buku na kusegula zosindikizira zake."
\v 3 Palibe aliyense kumwamba, padziko la pansi kapena pansi pa dziko yemwe anali oyenera kusegula buku kapena kuwerenga. \v 4 Ninalira maningi chifukwa panalibe aliyense oyenera kusegula kapena kuwerenga buku. \v 5 Koma m'mozi wa akulu-akulu anati kwa ine, "Usalire. Ona! nkhalamu ya mtundu wa ayuda, muzu wa Davide, wapambana. Akwanisa kusegula buku na kusegula zosindikizira zake."

View File

@ -73,6 +73,17 @@
"03-12",
"03-14",
"03-17",
"03-19",
"03-21",
"04-title",
"04-01",
"04-04",
"04-06",
"04-07",
"04-09",
"05-title",
"05-01",
"05-03",
"10-01",
"10-03",
"10-05",