Thu Apr 18 2024 15:49:09 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
b6825dcb0d
commit
6c1d849ff2
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 18 Iwo anachoka ku Midyani n’kukafika ku Parana, kumene anatenga amuna n’kupita nawo ku Iguputo kwa Farao mfumu ya Iguputo, amene anam’patsa nyumba ndi malo ndi chakudya. \v 19 Farao anamkomera mtima kwambiri Hadadi, moti Farao anampatsa mkazi, mlongo wake wa mkazi wake, mlongo wake wa Tapenesi mfumukazi.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 14 \v 1 Pa nthawiyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala kwambiri. \v 2 Yerobiamu anati kwa mkazi wake, Nyamukatu, udzizimbale, kuti usadziwike kuti ndi mkazi wanga, nupite ku Silo, popeza Ahiya mneneri ali komweko; ndiye amene ananena za ine, kuti ndidzakhala mfumu. \v 3 Utenge mitanda ya mikate khumi, mikate ndi mtsuko wa uchi ndipo upite kwa Ahiya.
|
Loading…
Reference in New Issue