nya-x-nyanja_1ki_text_reg/14/01.txt

1 line
353 B
Plaintext

\c 14 \v 1 Pa nthawiyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala kwambiri. \v 2 Yerobiamu anati kwa mkazi wake, Nyamukatu, udzizimbale, kuti usadziwike kuti ndi mkazi wanga, nupite ku Silo, popeza Ahiya mneneri ali komweko; ndiye amene ananena za ine, kuti ndidzakhala mfumu. \v 3 Utenge mitanda ya mikate khumi, mikate ndi mtsuko wa uchi ndipo upite kwa Ahiya.