diff --git a/11/18.txt b/11/18.txt new file mode 100644 index 0000000..08f2584 --- /dev/null +++ b/11/18.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 18 Iwo anachoka ku Midyani n’kukafika ku Parana, kumene anatenga amuna n’kupita nawo ku Iguputo kwa Farao mfumu ya Iguputo, amene anam’patsa nyumba ndi malo ndi chakudya. \v 19 Farao anamkomera mtima kwambiri Hadadi, moti Farao anampatsa mkazi, mlongo wake wa mkazi wake, mlongo wake wa Tapenesi mfumukazi. \ No newline at end of file diff --git a/14/01.txt b/14/01.txt new file mode 100644 index 0000000..3d1caf0 --- /dev/null +++ b/14/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 14 \v 1 Pa nthawiyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala kwambiri. \v 2 Yerobiamu anati kwa mkazi wake, Nyamukatu, udzizimbale, kuti usadziwike kuti ndi mkazi wanga, nupite ku Silo, popeza Ahiya mneneri ali komweko; ndiye amene ananena za ine, kuti ndidzakhala mfumu. \v 3 Utenge mitanda ya mikate khumi, mikate ndi mtsuko wa uchi ndipo upite kwa Ahiya. \ No newline at end of file