nya-x-nyanja_luk_text_reg/06/12.txt

1 line
247 B
Plaintext

\v 12 \v 13 Chinabwela chachitika masiku yaja nichakuti anaenda kuluphiri kupempela. Anapitiliza kupempela kwa Mulungu usiku onse. Pamene kunali muzuba, anaitana opunzila bake, ndiponso anasankha kumi ndi tuwili bamene analikuitana ati maapostoli.