Fri Nov 09 2018 16:34:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 16:34:44 +02:00
parent 70ef243926
commit 646486cfa6
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 Koma na Mikayeli mukulu wa angelo, pamene enze kusushanya na Satana pa tupi ya Mose sana yese kumuuza choyipa yayi. Koma anamuuza kuti, "Ambuye akukalipila!" \v 10 Koma aba bantu ba makamba vo kambakamba pa zitu zilizonse zamene sibaziba mushe. Ndipo baziba chabe - vamene ma imbwa osaganiza amaziba kupitila muchibadwire - ivi ndiye vinabaononga. \v 11 Soka kwa eve! Chifukwa banayenda njila ya Kaini, ndipo banizingenesa muku lakwa kwa Balaamu kofuna ndalama. Banaonongekela mu kupanduka kwa Korah.
\v 9 Koma na Mikayeli mukulu wa angelo, pamene enze kusushanya na Satana pa tupi ya Mose sana yese kumuuza choyipa yayi. Koma anamuuza kuti, "Ambuye akuzuzule!" \v 10 Koma aba bantu ba makamba vo kambakamba pa zitu zilizonse zamene sibaziba mushe. Ndipo baziba chabe - vamene ma imbwa osaganiza amaziba kupitila muchibadwire - ivi ndiye vinabaononga. \v 11 Soka kwa eve! Chifukwa banayenda njila ya Kaini, ndipo banizingenesa muku lakwa kwa Balaamu kofuna ndalama. Banaonongekela mu kupanduka kwa Korah.