Fri Nov 09 2018 21:49:42 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 21:49:43 +02:00
parent bec68060c8
commit 9cd6f45b86
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 4 \v 1 Okondewa,osakululupira muzimu olionse,koma yesani mizimu zonse kuziba ngati ichokela kuli mulungu,cifukwa aneneli aboza agena muziko. \v 2 Pali ichi muzaziba muzimu wa mulungu-muzimu ulionse wamene uzavomela kuti Yesu Kristu anabwela mu munthu achokela kuli mulungu, \v 3 ndiponso muzimu alionse wamene siuvomela Yesu siuchokela kuli mulungu. Uyu nimuzimu osusana na kristu,wamene munanvela ati ubwela,ndiponso unabwela kudala.