nya-x-nyanja_rev_text_reg/20/11.txt

1 line
385 B
Plaintext
Raw Permalink Normal View History

\v 11 ninaona mupando waukulu oyera na wamene anankhalapo. ziko lapansi na kumwamba kunathaba ulemelero wake, koma kunalibe malo yakuti zibisameko. \v 12 ninaona omwalira-ba mphamvu na opanda nchito-kuimilira pa mpando wa mfumu, mabuku yanaseguliwa. buku inangu inaseguliwa-buku la moyo. banthu bakufa banaweruziwa kulingana na zamene zinalembewa mu mabuku, kulingana na zinchito zawo.