nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/08.txt

1 line
250 B
Plaintext

\v 8 Pali phokoso pali okondewa wanga! Mvelani, apa abwela, akudumpha pamapili, nakujumpha pamapili. \v 9 Okondewa wanga ali kwati mbawala kapena mwana wa mphoyo; onani, wayimilila kuseli kwa khoma yathu, akuyang'anisisa pazenela, asuzumila pazenela.