Thu Oct 07 2021 13:44:18 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 13:44:18 +02:00
parent f256c7e1ad
commit a464b0f252
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
02/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Wokondedwa wanga anandiuza, nati, Dzuka, bwenzi langa; wokongola wanga, tiye, \v 11 tiwone, kuti dzinja lapita, mvula yapita, natha.

1
02/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Maluwawo awonekera padziko lapansi; nthawi yodulira ndi kuimba kwa mbalame yafika, ndipo phokoso la nkhunda lamveka m'dziko lathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu upsa nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita.

1
02/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Nkhunda yanga, m'matanthwe a thanthwe, ndi m'mapanga a m'matanthwe, ndionetseni nkhope yanu. Ndimve mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma, nkhope yako ndi yokongola. "Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo

1
02/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Tigwirire nkhandwe, nkhandwe zazing'ono zomwe zimawononga minda yamphesa, chifukwa munda wathu wamphesa uli ndi maluwa.

View File

@ -50,6 +50,10 @@
"02-01",
"02-03",
"02-05",
"02-07"
"02-07",
"02-08",
"02-10",
"02-12",
"02-14"
]
}