diff --git a/02/10.txt b/02/10.txt new file mode 100644 index 0000000..b382d29 --- /dev/null +++ b/02/10.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 10 Wokondedwa wanga anandiuza, nati, Dzuka, bwenzi langa; wokongola wanga, tiye, \v 11 tiwone, kuti dzinja lapita, mvula yapita, natha. \ No newline at end of file diff --git a/02/12.txt b/02/12.txt new file mode 100644 index 0000000..6ff4d58 --- /dev/null +++ b/02/12.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 12 Maluwawo awonekera padziko lapansi; nthawi yodulira ndi kuimba kwa mbalame yafika, ndipo phokoso la nkhunda lamveka m'dziko lathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu upsa nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita. \ No newline at end of file diff --git a/02/14.txt b/02/14.txt new file mode 100644 index 0000000..dc956a9 --- /dev/null +++ b/02/14.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 14 Nkhunda yanga, m'matanthwe a thanthwe, ndi m'mapanga a m'matanthwe, ndionetseni nkhope yanu. Ndimve mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma, nkhope yako ndi yokongola. "Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo \ No newline at end of file diff --git a/02/15.txt b/02/15.txt new file mode 100644 index 0000000..01e1413 --- /dev/null +++ b/02/15.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 15 Tigwirire nkhandwe, nkhandwe zazing'ono zomwe zimawononga minda yamphesa, chifukwa munda wathu wamphesa uli ndi maluwa. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index de58162..577593f 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -50,6 +50,10 @@ "02-01", "02-03", "02-05", - "02-07" + "02-07", + "02-08", + "02-10", + "02-12", + "02-14" ] } \ No newline at end of file