Thu Oct 07 2021 13:56:22 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 13:56:23 +02:00
parent 6fc1de8f33
commit 08f891f0b2
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
05/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 5 \v 1 Ndalowa m'munda mwanga, mlongo wanga, mkwatibwi wanga; Ndasonkhanitsa mure wanga ndi zonunkhiritsa zanga. Ndadya chisa changa cha uchi ndi uchi wanga. Ndamwa vinyo wanga pamodzi ndi mkaka wanga. imwani ndi kuledzera ndi chikondi.Mkazi amalankhula yekha

1
05/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Ndinali mtulo, koma mtima wanga unali maso. Pali phokoso la wokondedwa wanga akugogoda ndikunena, "Nditsegulire, mlongo wanga, wokondedwa wanga, nkhunda yanga, wanga wosadetsedwa, pakuti mutu wanga wanyowa ndi mame, tsitsi langa ndi chinyontho cha usiku."

1
05/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 "Ndavula mkanjo wanga; ndiyeneranso kuuvekanso? Ndasambitsa mapazi anga; kodi ndiwadetse?" \v 4 Wokondedwa wanga analowetsa dzanja lake pakhomo la chitseko, ndipo mtima wanga unakhudzidwa chifukwa cha iye.

1
05/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Ndidadzuka kuti ndimutsegulire wokondedwa wanga; manja anga anali kutulutsa mure, zala zanga ndi mule wonyowa, pachipata cha chitseko.

View File

@ -75,6 +75,10 @@
"04-10",
"04-12",
"04-15",
"05-title"
"05-title",
"05-01",
"05-02",
"05-03",
"05-05"
]
}