From 08f891f0b276d1f6780e5fc3b5219d0ebf0fa83c Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: tsDesktop Date: Thu, 7 Oct 2021 13:56:23 +0200 Subject: [PATCH] Thu Oct 07 2021 13:56:22 GMT+0200 (Central Africa Time) --- 05/01.txt | 1 + 05/02.txt | 1 + 05/03.txt | 1 + 05/05.txt | 1 + manifest.json | 6 +++++- 5 files changed, 9 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 05/01.txt create mode 100644 05/02.txt create mode 100644 05/03.txt create mode 100644 05/05.txt diff --git a/05/01.txt b/05/01.txt new file mode 100644 index 0000000..790ba77 --- /dev/null +++ b/05/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 5 \v 1 Ndalowa m'munda mwanga, mlongo wanga, mkwatibwi wanga; Ndasonkhanitsa mure wanga ndi zonunkhiritsa zanga. Ndadya chisa changa cha uchi ndi uchi wanga. Ndamwa vinyo wanga pamodzi ndi mkaka wanga. imwani ndi kuledzera ndi chikondi.Mkazi amalankhula yekha \ No newline at end of file diff --git a/05/02.txt b/05/02.txt new file mode 100644 index 0000000..3ede1e9 --- /dev/null +++ b/05/02.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 2 Ndinali mtulo, koma mtima wanga unali maso. Pali phokoso la wokondedwa wanga akugogoda ndikunena, "Nditsegulire, mlongo wanga, wokondedwa wanga, nkhunda yanga, wanga wosadetsedwa, pakuti mutu wanga wanyowa ndi mame, tsitsi langa ndi chinyontho cha usiku." \ No newline at end of file diff --git a/05/03.txt b/05/03.txt new file mode 100644 index 0000000..2ce74b4 --- /dev/null +++ b/05/03.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 3 "Ndavula mkanjo wanga; ndiyeneranso kuuvekanso? Ndasambitsa mapazi anga; kodi ndiwadetse?" \v 4 Wokondedwa wanga analowetsa dzanja lake pakhomo la chitseko, ndipo mtima wanga unakhudzidwa chifukwa cha iye. \ No newline at end of file diff --git a/05/05.txt b/05/05.txt new file mode 100644 index 0000000..01a3138 --- /dev/null +++ b/05/05.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 5 Ndidadzuka kuti ndimutsegulire wokondedwa wanga; manja anga anali kutulutsa mure, zala zanga ndi mule wonyowa, pachipata cha chitseko. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index bd1514e..862a369 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -75,6 +75,10 @@ "04-10", "04-12", "04-15", - "05-title" + "05-title", + "05-01", + "05-02", + "05-03", + "05-05" ] } \ No newline at end of file