nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/05.txt

1 line
310 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 5 Ndine ofipa koma wokondewa, ana akazi imwe a ku Yerusalemu; ofipa ngati mahema ya Kedara, okongola ngati nsalu za Solomoni. \v 6 Musaniyang'ane chifukwa ndine ofipa, chifukwa zuba ya shoka ine. wana mwuna wanga anakalipa naine; Banani ika oyang'anila minda yamphesa, koma sininasunge munda wanga wamphesa.