2017-10-01 18:58:54 +00:00
|
|
|
\v 5 Ndine ofipa koma wokondewa, ana akazi imwe a ku Yerusalemu; ofipa ngati mahema ya Kedara, okongola ngati nsalu za Solomoni. \v 6 Musaniyang'ane chifukwa ndine ofipa, chifukwa zuba shoka ine. mwana mwuna wanga anakalipa naine; Banani ika oyang'anila minda yamphesa, koma sininasunge munda wanga wamphesa.
|