1 line
256 B
Plaintext
1 line
256 B
Plaintext
|
\v 6 Ndiike pamtima pako ngati chisindikizo, ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi nchamphamvu ngati imfa. Kudzipereka kosalamulirika kuli kosalekeza monga Manda; malawi ake anaphulika; ndi lawi lamoto, lawi loyaka moto koposa moto wina uliwonse.
|