1 line
185 B
Plaintext
1 line
185 B
Plaintext
|
\v 12 Tidzuke m'mawa kuti tipite kuminda yamphesa; tiwone ngati mipesa yaphuka, kaya maluwa ake atseguka; kapena ngati makangaza ali ndi maluŵa. Kumeneko ndidzakupatsa chikondi changa.
|