2017-10-01 20:48:52 +00:00
|
|
|
\c 3 \v 1 Usiku nili pa bedi yanga nenze kulakalaka wamene moyo wanga ukonda; Nina mfunafuna, koma sinina mupeze. \v 2 Nina zikambisa neka, "Niza uka naku kupyola pakati pa mzinda, kupyolela mu misewu na muma bwalo; niza fufuza wamene moyo wanga umkonda." Nina mfunafuna koma sinina mupeze.
|