2017-10-01 20:46:55 +00:00
|
|
|
\c 3 \v 1 Usiku nili pa bedi yanga nenze kulakalaka wamene moyo wanga ukonda; Ninamfunafuna, koma sininamupeze. \v 2 Ninazikambisa neka, "Niza uka naku kupyola pakati pa mzinda, kupyolela m'misewu na mumabwalo; nizafufuza wamene moyo wanga umkonda." Ninamfunafuna koma sininamupeze.
|