Thu Jan 24 2019 20:57:35 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 20:57:36 +02:00
commit dcc014a9fb
26 changed files with 27 additions and 1 deletions

1
14/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 14 \v 1 \v 2 Ninaona na kuona mwana wa nkhosa oimilira pa phiri la Zion. Anali na anthu 144,000 amene anali na zina lake na zina la Atate ake yolembewa pa mphumi zao. Ninamvera mau ochokera kumwamba omveka monga manzi yambiri na kugunda kwa mphamvu. Mau omwe ninamvera yanali monga anthu oliza mitoliro.

1
14/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda chifukwa.

1
14/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Ninaona mngelo wina akuuluka mu mwamba, amene anali na uthenga wa moyo ouza anthu onkhala pa ziko la pansi-ku maiko onse, mitundu yonse, chilankhulo na anthu. Anaitana na mau a mphamvu, "yopani Mulungu na kumupasa ulemelero. Chifukwa nthawi ya chiweruzo chake chafika. Mulambileni, wamene anapanga kumwamba, dziko la pansi, nyanja, na nyenje za manzi."

1
14/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Mngelo wina-mngelo wachiwiri- anasatira kukamba kuti, "Wagwa, wagwa Babylon wamphamvu, wamene anauza anthu onse kuti amwe vinyo wa zilakolako zake za chiwelewele."

1
14/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 Mngelo wina-mngelo wachitatu- anawalondola kukamba ati na mau okuwa, "ngati wina apembeza chilombo na chifano chake, na kupasiwa namba pa mphumi kapena pa zanja lake, azamwa vinyo wa mkwiyo wa Mulungu, vinyo wamene waikiwa opanda kutirako manzi mu cup ya kukalipa kwake. Munthu amene azamwa azabvutika na muliro na sufule pamenso pa angelo na mwana wa nkhosa."

1
14/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 \v 12 Utsi wa kunzunzika kwao upitilira ku mwamba nthawi zonse, ndipo sapumula usana na usiku-awa opembeza chilombo na fano lake, na aliyese amene analandira chizindikiro cha zina lake. Apa pali kufunika kupilira kwa iwo amene ni oyera, amene akonkha malamulo ya Mulungu na chikhulupiliro mwa Yesu."

1
14/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Ninamva mau kuchoka ku mwamba kukamba ati, "Lemba izi: Odala ni anthu amene anafa mwa ambuye." "Inde," ukamba mzimu,"kuti akapumule ku zolemesa zao, chifukwa nchito zao zizabalondola."

1
14/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 \v 15 \v 16 Ninayangana, ndipo panali makumbi yoyera. Ndipo onkhala pa makumbi anali ngati mwana wa munthu. Anali na kolona ya golide pa mutu pake na chikwakwa chonola ku manja yake. Ndipo mngelo wina anatuluka mu nyumba ya Mulungu ndipo anaitana na mau okweza kuitana uja amene ali pa makumbi: "Tenga chikwakwa chako elo uyambe kujuba. Chifukwa nthawi yojuba yakwana, cifukwa zokolola pa ziko zapya." Ndipo wamene anali pa makumbi anayamba kuyendesa chikwakwa pa ziko, ndipo ziko inakololedwa.

1
14/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 \v 18 Mngelo wina anatuluka ku mwamba mu nyumba ya Mulungu; nayeve anali na chikwakwa. Mngelo winanso anatuluka kuchoka pa guwa la zonunkhirisa, amene anali na ulamuliro pa muliro. Anaitana na mphamvu uja amene anali na chikwakwa chonola, "Tenga chikwakwa chako na kuika pamozi zidunswa za mpesa m'minda ya ziko, chifukwa mpesa wake wapya."

1
14/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 \v 20 Mngelo anayendesa chikwakwa chake pa ziko nakutenga zidunswa za mpesa. Anaiponya motwera mpesa wa mkwiyo wa Mulungu. Ndipo motwera mpesa munaponyewa panja pa mzinda, ndipo magazi anathiridwa kuchoka mwaicho kufika pakamwa pa akavalo, ma stadia 1,600.

1
14/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 14

1
15/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 15 \v 1 Ndipo ninaona chizindikiro china m'mwamba, zazikulu ni zabwino: Panali angelo 7 ni mikwiyo 7, yamene ni zilango zothera, chifukwa mwa izi mkwiyo wa Mulungu uzatha.

1
15/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Ninaona chamene chinaoneka monga nyanja ya galasi yosakaniza na muliro. Amene anaimilira pa mbali ya nyanja ni aja amene anapambana chilombo na fano lake, na nambala yamene iimilira zina lake. Anali na mitoliro yamene anapasidwa na Mulungu.

1
15/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 Anali kuimba nyimbo ya Mose, kapolo wa Mulungu, nyimbo ya mwana wa nkhosa: "Nchito zanu ni zabwino komanso za mphamvu, ambuye Mulungu, wa mphamvu zonse. Njira zanu ni zabwino ni za chilungamo, mfumu ya maiko onse. Ndani wamene sazakuyopani, Ambuye, nakukweza zina lanu? Chifukwa inu nokha ndinu oyera. Maiko onse yazabwera kukupembezani cifukwa cha nchito zanu zoyera zomwe zavumbulusidwa."

1
15/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 \v 6 Pambuyo pa izi zinthu ninaona, ndipo tenti ya mboni inaseguliwa ku mwamba. Kuchoka pa malo oyera panachoka angelo 7 onyamula zilango 7. Anavala zobvala zoyera, zonyezimila ndi sashi ya golide yozungulira chifuwa chao.

1
15/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 Imozi mwa zamoyo zinai inapasa angelo 7 mbale za golide 7 za mkwiyo wa Mulungu, zamene zinkhala muyayaya. Tempile inazaziwa na utsi wa ukulu wa Mulungu na mphamvu zake. Palibe amene analobamo mpaka pamene zilango zonse 7 zinatha.

1
15/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 15

1
16/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 16 \v 1 Ninamvera mau amphamvu kuchoka mu tempile ya Mulungu kuuza angelo 7, "pitani muthire mbale 7 za mkwiyo wa Mulungu."

1
16/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Mngelo oyamba anapita na kuthira mbale yake pa ziko; zilonda zoipa ni zobaba zinachoka pa anthu amene anali na chizindikiro cha chilombo, amene anapembeza fano lake.

1
16/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Mngelo wachiwiri anathira mbale yake mnyanja. Inasanduka magazi, monga magazi ya munthu wakufa, ndipo chilichonse cha moyo mu manzi chinafa.

1
16/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 \v 7 Mngelo wa chitatu anathira mbale yake m'misinje na nyenje za manzi ndipo zinasanduka magazi. Ninamvera mgelo wa manzi kukamba ati, "ndinu oyera-amene aliko ndipo analiko, Oyera- chifukwa mwaweruza zinthu izi. Chifukwa anathira magazi ya okhulupilira na aneneri, mwabapasa magazi kuti bamwe; ni zamene bayenera. Ninamvera guwa kukamba ati, "Inde, ambuye Mulungu a mphamvu zonse, chiweruzo chanu ni ca zoona na cholungama."

1
16/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 \v 9 Mngelo wa chinai anathira mbale yake ku zuba, ndipo inapasidwa chilolezo chotentha anthu na muliro. Anatenthedwa na kupya kwakukulu, ndipo ananyoza zina la Mulungu, amene ali na mphamvu pa ziwawa zimenezi. Sibanalape kapena kumupasa ulemelero.

1
16/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 \v 11 Mngelo wa cisanu anathira mbale yake pa mpando wa chilombo, ndipo mdima unaphimba umfumu wake. Anakukuta malilime ao chifukwa cha kuwawa. Ananyoza zina la Mulungu chifukwa cha kuwawa na zilonda, koma anakana kulapa zoipa zomwe anali kuchita.

1
16/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 \v 14 Mngelo wa nambala 6 anathira mbale yake mu msinje waukulu wa Euphrates. Manzi yake yanauma kupanga njira ya mamfumu yamene yanachokera ku m'mawa. Ninaona mizimu yoipa yomwe yanaoneka monga achule kutuluka mkamwa mwa chinjoka, mwa chilombo na mwa mneneri wa boza. Chifukwa ni mizimu ya ziwanda kuchita milakuli ni zizindikiro. Anali kupita kwa mamfumu a ziko lonse kuwasonkhanisa pamozi kukonzekera nkhondo pa siku lalikulu la ambuye amphamvu zonse.

1
16/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 16

View File

@ -35,7 +35,8 @@
"translators": [
"Alpen Banda",
"Jane Kuntashula",
"moses zulu"
"moses zulu",
"GEORGE NKHOMA"
],
"finished_chunks": [
"11-title",