nya-x-nyanja_mrk_text_reg/05/35.txt

1 line
188 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 35 Pamene anali kulankhula naye, anthu ena anabwela kucokela kunyumba ya uja mtsogoleli wa sunagogi, nati, "mwana wanu mkazi wamwalila. Cifukwa ncani mupitiliza kumuvutisha mphunzitsi?"