Thu Jul 30 2020 10:36:06 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
commit
7cf1b4e3f4
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 1 \v 1 Ici ndiye ciyambi ca nkani yabwino ya Yesu Kristu, Mwana wa Mulungu. \v 2 Monga vinalembewa na Mneneri Yesaya," Onani nituma Kapaso wanga pamenso panu, wamene azakonza njila yanu. \v 3 Mau ya uyo opunda msanga, 'Konzani njira ya Ambuye; mupangileni njila ilibe makona."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 4 Yohane anabwera, nakubatiza msanga nolalikila za ubatizo olapa paku khululukidwa kwa macimo. \v 5 Ziko yonse ya Yudeya na anthu onse aku Yerusalemu anayenda kuli yeve. Anabatiziwa na eve mumana wa Yolodani, nakuvomela macimo yawo. \v 6 Yohane anzovala zovala zausako wa ngamila na beluti ya cikumba mumsana mwake, ndipo anali kudya nthete na uchi wamusanga.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 7 Analalikila, "Winangu alikubwela pambuyo panga wamene ali wamphavu kupambana ine, ndipo sindiyenela kubelama kumangusula ntambo yansapato zake. \v 8 Ine nikubatizani na manzi, koma iye azakubatizani imwe na Mzimu Woyela."
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 9 Vinacitika ivi mumasiku aja pamene Yesu acacokera ku Nazalete mu Galileya, ndipo anabatiziwa na Yohane m'mumana wa Yolodani. \v 10 Pamene Yesu anacoka mumanzi, anaona kumwamba kwa seguka na Mzimu ulikuseluka mowoneka ngati kunda.
|
||||
\v 11 Na mau anacokela kumwamba nati, "Ndiwe mwana wanga wenikonda. Ndi kondwela nawe."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Ndipo Mzimu unampeleka yeve kuyenda kusanga. \v 13 Enze msanga kwa masiku 40, kuyesewa na satana. Anali na nyama za msanga, na Angelo kumtumikila eve.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 14 Manje pamene Yohane anamangiwa, Yesu anabwele ku Galileya alikulalikila uthenga wa Mulungu, \v 15 elo enzokamba ati, "Nthawi yakwana, ndipo ufumu wa Mulungu uli pafupi. Lapani ndipo mkhulupilile mu uthenga."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 16 Pamene enzokuyenda mumbali mwa kamana ka Galileya, anaona Simoni na Anduleya mbale wa Simoni alikukuponya kombe muchimana, cifukwa anali ogwira nsomba. \v 17 Yesu anabauza ati, " Bwelani, nikonkheni, ndipo ndizakupangani ogwira anthu." \v 18 Ndipo pamene apo anasiya makombe nomukonkha.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 19 Pamene Yesu anayendako cabe pang'ono, anaona Yakobo mwana wa Zebediya na Yohane mbale wake; anali muboti alikutunga makombe. \v 20 Anabaitana ndipo anasiya Atate awo Azebediya na a nchito muboti, nakumukonka.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 21 Ndipo anafika ku kapenamu, ndipo pa sabata, Yesu anangena musunagoge nophunzisa. \v 22 Anadabwa navenzeli kuphunzisa, analikuphunzisila ngati munthu anali na ulamuliro osati nga na alembi.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 23 Pamene apo munali munthu musunagoge enze na mizimu yoipa yamene inalila \v 24 nati, "Nanga tinambali bwanji naiwe, Yesu waku Nazareti? Wabwela kutiononga? Nikuziba iwe. Niwe woyela wa Mulungu!" \v 25 Yesu anakalipila dimoni nati, " Siya kukamba ndipo coka mwaiye!" \v 26 mzimu woipa unamgwesa pansi nakucoka mwa iye ulikulila mokuwa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 27 Ndipo anthu wonse anadabwa, ndipo anafunsana wina ndi muzake, " Nanga ici nicani? Ciphunziso casopano cina ulamulilo? Alamulila na mizimu yoipa ndipo imumvelela!" \v 28 Mbili yake inamveka pali ponse mumzinda wonse wa ku Galileya.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 29 Pamene anacoka musunagoge, anangena munyumba ya Simoni na Andeleya pamodzi na Yakobo na Yohane. \v 30 Manje apongozi a Simoni enze gone odwala mphepo, anamuuza Yesu za iye. \v 31 Ndipo Yesu anabwela, anamugwila pa kwanja , nakumunyamula; mphepo inacoka, ndipo anayamba kubapasa vakudya.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 32 Mazulo mwake, pamene zuba inangene , anabwelesa kwake wonse odwala nabamene enze naviwanda. \v 33 Muzinda wonse unasonkhana panja pa ciseko. \v 34 Anacilisa ambiri enze odwala matenda wosiyana-siyana nocosa madimoni ambiri, koma sanavomeleze madimoni kuti yakambe cifukwa yanamuziwa iye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 35 Anauka kuseni-seni, kukali kofipa; anacoka nakuyenda kumalo kwayeka ndipo anapemphela kwamene kuja. \v 36 Simoni na aja enze naye anamusakira. \v 37 Anamupeza nakumuuza kuti, "Anthu wonse asakila iwe."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 38 Iye anati, "Tiyeni tiyende kwina, kumizinda inangu, kuti nikalalikileko nakweve. Nicifukwa cake nina bwela kuno." \v 39 Anayenda malo yonse ya Galileya, kulalikila mumasunagoge yawo nakucosa madimoni.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 40 Munthu wolwala makate anabwela kwa yeve. Anali kupempha iye; anagwada pansi nakuti, "Ngati mufuna, munganitubise" \v 41 Yesu anamvela cifundo, nakumugwila nakwanja kwake nati, "Ndifuna, kuyelesewe." \v 42 Pamene apo makate anacoka iye, ndipo anapola.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 43 Yesu anamucenjeza maningi nakumuuza ati ayende \v 44 Anati kwa yeve, "usayese kuuza munthu aliyense, koma yenda ukazilangize kwa wansembe, ndipo ukapeleke nsembe yakukuyelesela ija yamene analamulila Mose, ngati umboni kwa beve."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 45 Koma anayenda nayamba kuuuza aliyense nopeleka nkhani nopangisa kuti Yesu asakwanise kungena momasuka m'muzinda uliwonse. Ndipo anankhala ku malo kunalibe anthu enzonkhalako ndipo anthu anabwela kuli eve kucokela kosiyana-siyana.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 1
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 2 \v 1 Manje pamene anabwelako ku kapenamu, patapita pa masiku yang'ono, inamveka mbili kuti ali panyumba. \v 2 Ndipo ambili anabwela kwamene anali kuti malo yonse yanazula, na pa komo ponse, ndipo Yesu analankhula nawo mau.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Ndipo amuna ena anabwela kwa iye ananyamula mwamuna wozizila mubili, Amuna anai anamunyamula iye. \v 4 Pamene analepela kufika pafupi ndi iye cifukwa ca nyamutindi wa anthu, anapasula mutenje wanyumba pamene analili. Ndipo anakumba zenje, anaingenesa mpasa pamene panali munthu wozizila mubili.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 5 Pakuona chikhulupirilo cawo, Yesu anati kwa uja wozizila mubili, " Mwana wanga, macimo yako yakhululukiwa. \v 6 "Manje alembi ena enze anali nkale pamene paja, banaganiza mkati mwamitima yawo, \v 7 "Uyu anagakambe bwanji telo? Alikonyozela! Ndani angakululukile macimo koma Mulungu cabe?
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 8 Yesu ananziba mwamusanga m'mzimu wake vamene benzoganiza, Anati kwa iyo, "Cifukwa nicani mulikuganiza motelo mmitima yanu? \v 9 Capafupi nicabwanji kunena kuli wozizila mubili kuti, 'Macimo yako yakhululukiwa' kapena kulankhula kuti 'Ima, Tenga mpasa yako, yenda?'
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 Koma kuti muzibe kuti mwana wa Munthu ali ulamulilo pa dziko yapansi yokhululukila macimo, "anati kuli uja wozizila mubili, " \v 11 Nikuti kuli iwe, ima, tenga mpasa yako, pita kunyumba kwako." \v 12 Anayima pamene apo, nakuthenga mpasa nakuyenda ku nyumba kwake pakazanga ka anthu, ndipo wonse anadabwa ndi kupeleka ulemelero kwa Mulungu, nati, "Tenze tikalibe kuonapo vya so."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 13 Anayendanso pa chimana, ndipo anthu wonse anaza kwa iye, ndipo anabaphunzitsa. \v 14 Pamene ali kupita anaona Levi mwana wa Alefa alinkhale posonkhela msonkho ndipo iye anati, "Unikonkhe ine" anaima nakumukonkha iye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 15 Ndipo pamene Yesu anali kudya munyumba ya Levi, ambiri wosonkhesa msonkho ndi wocimwa banali kudya naye Yesu ndi wophunzila ake, chifukwa anali ambiri amene anali kumukonkha. \v 16 Pamene alembi, amene anali Afalisi, anaona kuti Yesu anali kudya pamodzi ndi wocimwa ndi wosonkhesa msonkho, anati kwa wophunzila ake, "Chifukwa niciani ali kudya pamodzi ndi wosonkhesa msonkho ndi anthu wocimwa?"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 17 Pamene Yesu anamvwa izi anati kwa iwo, " Anthu wolimba mthupi samafuna dokotala; koma iwo amene ali wodwala amafuna dokotala. Sindinabwele kuzoitana anthu wolungama, koma anthu wocimwa."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 18 Wophunzila a Yohane ndi Afalisi anali kusala kudya. Ndipo anthu ena anaza ndikunena kwa iye, " Chifukwa nicani wophunzila a Yohane alikusala kudya, koma wophunzila anu salikusala kudya?" \v 19 Yesu anati kwa iwo, "Kodi wobwela ku cikwati angasale kudya pamene mwine ukwati ali nawo pamodzi? maka-maka ngati mwine wa ukwati alipo sangasale kudya.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 20 Koma masiku yazabwela pamene mwine ukwati azatengedwa pakati pawo, pamasiku ayo, azakasala kudya. \v 21 Palibe amene amasokha nyula yanyowani pa cigamba ca kale, ngati acita telo cigamba cizang'ambika, canyowani cizang'amba ca kale, ndipo cizang'amba kwambiri.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 22 Kulibe amene amaikha vinyo wa lomba muthumba ya vinyu yakale, ngati acita telo thumba ya vinyu ipulike ndipo zonse vinyu ndi thumba ya vinyu izaonongeka. Cofunika ni kuika vinyu wa nyowani mu thumba ya vinyu ya nywani."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 23 Pa siku ya Sabata Yesu analikupita pakati ka munda wa tiligu, ndipo wophunzila ake anayamba kutyola mitu ya tiligu. \v 24 Ndipo Afalisi anati kwa iye, " Onani, Chifukwa nicani alikucita zamene lamulo la sabata silivomeleza?"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 25 Iye anati kwa iwo, "Kodi simunabelengepo zamene Davide anacita pamene anali ndi njala ndi kufunisisa kudya - ndi anthu amene anali naye- \v 26 mwamene anayendela mu nyumba ya Mulungu pamene Abithala anali Mkulu wansembe, ndipo anadya buledi ya mkati, camene sicinali covomelekezedwa ku munthu aliyense kocoselako cabe wansembe, ndipo iye anapasako ndi iwo amene anali nawo?"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 27 Yesu nati, " Sabata niya munthu osati munthu ankhale kapolo wa sabata. \v 28 Chifukwa cake, mwana wa Munthu ni mbuye wa Sabata."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 2
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 3 \v 1 Mobwezela anangenanso musunagoge munali mwamuna anali ndi zanja yofota. \v 2 Ena anthu anali kumuyangana kuti aone ngati azamucilisa pa sabata kuti amupase mlandu.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Yesu anati kuli uja munthu wofota kwanja, " Ima, Imilila pakati pa wonse." \v 4 Ndipo anati ku anthu, " Kodi ndicovomelekezeka kucita cabwino pa siku ya Sabata kapena kucita cinthu coyipa; kupulumusa moyo, kapena kupaya?" Ndipo onse anali cete.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 5 Anabayangana ndi ukali, ana kumudwisiwa ndi kuuma mtima kwawo, ndipo anati kumwamuna, "Tambulula kwanja kwako." Ndipo iye anatambulula, ndi zanja lake linankhala bwino. \v 6 Ndipo Afalisi panthawi yamene iyo anapita kukafuna-funa njila yompaila pamodzi ndi ma Helodiya.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 7 Ndipo Yesu, pamodzi ndi wophunzila , anayenda kuchimana, ndipo anthu ambiri anamukonkha kucokela ku Galileya ndi ku Yudeya \v 8 ndi kucokela ku Yelusalemu ndi ku Idumeya ndikupitilila Yorodani ndi kuzungulila Tireya ndi Sidoni. Pamene anamvwa pa zamene analikucita, anthu ambiri anaza kwa iye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 9 Ndipo anafunsa wophunzila ake kuti akonzeke kaboti kang'ono chifukwa anthu anali ambili, kuti osati azimuguma-guma. \v 10 Chifukwa anacilisa ambili, kuti aliyense amene anali wovutika anafuna-funa kuti afike kwa iye kuti amukuze.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 11 Nthawi zonse pamene mzimu woipa unamuona iye, unalikugwa pansi ndi kulira kokuwa, unali kunena ati, " Iwe ndiwe Mwana wa Mulungu." \v 12 Ndipo iye anali kuulesa kuti asamuzibe.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 13 Ndipo iye anakwela kulupili, ndi kuyitana aja amene anali kufuna, ndipo anaza kwa iye. \v 14 Anasankhapo bali twelufu (12), ( awo becipasa zina kuti ndi apositolo), kuti azinkhala naye ndipo kuti akabatume kuyolalikila uthenga. \v 15 ndi kukala ndi mpamvu zocosela vibanda.
|
||||
\v 16 Ndipo anasankhapo twelufu: (12) : Simoni uyo wecipasa zina yakuti Petulo;
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 17 Yakobo mwana wa Zebedayo, and Yohana na mbale wake Yakobo, awo wecipasa zina Bonenge kuthanthauza Bana na kaleza; \v 18 ndi Anduleya, Filipo, Batolomeyo, Mateyo, Thomase, Yakobo mwana wa Afalesi, Thadeyo, Simoni wa Zilote, \v 19 ndi Yudasi Iscariyoti, uja wamene emugulisa.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 20 Ndipo anayenda kunyumba, ndi anthu ambiri anaza futi pamodzi, ndikukana kudya buledi.
|
||||
\v 21 Pamene abanja ake anamvwa izi, anayenda kuti akamugwile, cifukwa anati, "waleka kuganiza bwino." \v 22 Alembi amane anabwela kucokela ku Yelusalemu anati, "ali na vibanda vya Beluzabebu," soti, "mwa ulamulilo wa vibanda ocosa vibanda,"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 23 Yesu anabaitana nati kwawo mwafanizo, "Zingacitike bwanji kuti Satana kucosa Satana? \v 24 Ngati ufumu niwogabanikana suungaimilile. \v 25 Ngati nyumba niyogabanikana, ila nyumba siingate kuimilila.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 26 Ngati Satana waziukila yeka ndipo wagabanikana, sangaimilile, koma uku kukuba kusila kwake.
|
||||
\v 27 Koma palibe amene angangene munyumba ya nyampamvu nakuba zonse zakeakaliye kumumanga ula nyampamvu, ndipo pambuyo pake niye pombela nyumba yake.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 28 \v 29 \v 30 Coonadi ndikuuzani , ucimo uliwonse wa mwana wa munthu uzakakhululukidwa, ndi minyozo yonse yokambidwa, koma aliwonse wonyoza Mzimu Woyela sazakakhululukidwa, koma azankhala wocimwa ndi ucimo wa nthawi zonse." Yesu anakamba izi cifukwa banali kukamba kuti, " Ali na mizimu yonyansa."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 31 Ndipo amai ake ndi abale ake anabwela nakuzoimilila panja. Banatuma banthu, nakumuitana. \v 32 Ndipo anthu ambiri analipo nankhala momuzungulila iye ndipo anati,"Amai anu ndi abale anu ali pabwalo, okusakilani,"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 33 Anabayankha nati,"Nanga amai anga ndi abale anga ndibati?" \v 34 Anayangana aja amene analinkhale omuzunguluka nati,"Onani, aba ndiye amai anga ndi abale anga! \v 35 Cifukwa aliwonse amene acita cifunilo ca Mlungu, uja munthu ndiye mbale wanga, ndiye mlongo ndipo mai wanga."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 3
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 4 \v 1 Nafuti anayamba kuphunzitsa mumbali ya chimana. Ndipo anthu ambiri anaza kwa iye, ndipo anasika mu boti inali pachimana, nakhala pansi. Anthu wonse anali kumbali kwa chimana. \v 2 Anabaphunzisa zinthu zambiri mumafanizo, ndipo anati kwawo muciphunzinso,
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Mvelani, mlimi anayenda kukafesa mbeu zake. \v 4 Pamene analikubyala, mbeu zina zinagwela munjila, mbalame zinabwela nakudya mbeu. \v 5 Mbeu zina zinagwela pamwala, panalibe doti yambili. Nthawi yamene zinangomela, cifukwa mizyu siinayende kwambili pansi pa doti.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 6 Koma pamene zuwa inacoka, zinapya, cifukwa zinalibe mizyu zinayuma. \v 7 Mbeu zina zinagwela mitengo ya minga. Mitengo ya minga inakula ndipo mbeu inalasidwa, ndipo siinabale mbeu iliyonse.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 8 Mbeu zina zinagwela panthaka yabwino ndipo zinabala zipaso pamene zinali kukula ndikuculuka, zina zinabala makumi yatatu (30), zina makumi asanu ndi imodzi (60), ndi zina makumi kumi (100)." \v 9 Ndipo anati, "uyo ali ndimakutu omvela, amve!"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 \v 11 \v 12 Pamene Yesu anali yeka, iwo amene anali naye pafupi ndi iye ndi aja twelufu anamufunsa iye za fanizo. Ndipo anati kwawo, "kuli imwezapasidwa zisinsi za ufumu wa Mlungu. Koma kwa iwo ali kunja zonse zili mumafanizilo, kuti pamene apenya, inde azapenya, koma sazaona, ndipo pamene azamva, inde zamva, koma sazamvesa, kuti angabwelele kuli Mlungu ndikubakhululukila macimo yawo."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 13 Ndipo anati kwa iwo, "Simvesesa fanizo iyi? Muzamvesesa bwanji mafanizo yena? \v 14 Mlimi amaene anafesa mbeu yake ndiye amane afesa mau. \v 15 Zina zimene zinagwela mbali mwa njila, mwamene mau anagwela. Ndi pamene amvela mau, Satana panthawi yamene iyo amabwela ndikutenga mau amene anafesedwa mwa iwo.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 16 Ndi zina zimene zinafesedwa pa mwala, ndi iwo amene amamva mau, nthawi yamene amalalikidwa mau amalandila ndi chimwemwe. \v 17 Ndipo alibe mizu mwa iwo, koma amalimbikila kwa kathawi kocepa. Pamene akumana ndi mabvuto kapena abanzunza cifukwa ca mau nthawi yamene ija amagwa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 18 \v 19 Ndipo zina zamene zinagwela pa minga. Amamva mau, \v 19 koma nkhawa ya zamudziko, chinyengo ca vya cuma, cilakolako ca vinthu vina cimabangena, cimaononga mau, ndipo amankhala opanda cipatso. \v 20 Ndipo zina zinja zamene zinafesedwa pa nthaka yabwino. Iwo amamva mau ndikulandila ndikubala zipatso; zina makumi yatatu(30) ndi zina makumi asanu ndi imozi(60) ndi zina makumi kumi (100)
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 21 Yesu anati kwa iwo, "Kodi mungabwelese \v 22 \v 23 Yesu
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 24 Anati kwa iwo, "Ikankhoni nzeru pa zimene mumvela, cifukwa ndimpimo wamene mupimilamo, azasebenzesya mupimo wamene uyo uzapasidwa kwanu. \v 25 Cifukwa aliwonse amene alinavo, kuli yeve zizapasidwa zambiri, ndi kuli uyo alibe , zizapokedwa cukanga zimene alinazo."
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 26 Ndipo anati, "Ufumu Pamene wa Mlungu uli ngati munthu amene anafesa mbeu yake pansi. \v 27 Pamene anagona usiku pamene anauka mmawa, mbeu inayamba kumela ndikukula, cukanga iye sanazibe zimene zinacitika. \v 28 Nthaka inayamba kubeleka zipatso: poyamba mpunga, pavuli pake mbeu.
|
||||
\v 29 Pamene inapya mumela nthawi yamene iyo anatuma bavikwakwa, cifukwa nthawi yokolola inafika."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 30 Ndipo anati, "Tizayelekeza ndiciyani ufumu wa Mlungu, kapena ndifanizo yabwanji yamene tizasebezesha kukamba? \v 31 uli ngati kambeu kampiru, kapene kanafesedwa, ndikang'ono kwambiri pambeu zonse pa dziko lapansi. \v 32 Koma pamene kafesedwa, ndikukula kamakala kakulu kupambana cimutemgo cilicose ca mdimba, ndipo kamankhala ndi misambo zikulu, ndipo mbalame zamumulenga-lenga zimabwela ndikumanga visa mucifule cake."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 33 Ndi mafanizo yambili yotelo anakamba mau kwa iwo, monga mwamene anamvesesa, \v 34 ndipo sanakambepo ciliconse kosasebenzesha fanizo, koma pamene anali yeka, anafotokoza zonse kwa wophunzila ake.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 35 Pa siku ija, pamene kunali mumazulo, anati kwa iwo, "Tiyeni kusidya ina," \v 36 Ndipo anasiya anthu ambiri, anayenda pamodzi ndi Yesu, cifukwa anali kale muboti. Ndipo maboti yena anali naye.
|
||||
\v 37 Ndipo cimphepo cikulu cinanyamuka mu boti, ndipo boti inazula kwambiri cifukwa ca mawevu.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 38 Koma Yesu iye anali pansi pa boti atagona pa kushoni. Ndipo anamuuusha nati, "Mphunzisi, kodi simusamalila kuti tili kufa?" \v 39 Ndipo, anauka, ndikuzuzula cimphepo cija nati kucimana, "Mtendele, nkala cete." Ndipo mphepo ija inaleka, ndipo kunali cete.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 40 Ndipo anabafunsa iwo, "Kodi ndiciyani munacita mantha? Kufikila tsopano mulibe cikhulupirilo?"
|
||||
\v 41 Anali ndi mantha yakulu ndipo anati kwa wina ndi mzace, " Nidani uyu, cukanga cimphepo na cimana cimumvelela iye?"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 4
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\c 5 \v 1 anabwela ku sidya ina ya chimana, kumuzinda wa Gelasene.
|
||||
\v 2 Ndipo panthawipamene Yesu analikucoka mu Boti, munthu wa vimizimu vyonyansa anabwela kucokela ku manda.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Munthu uja anali kunkhala ku manda. Kunalibe munthu aliyense amene anakwanisa kumulesa, cukanga macheni sanakwanise. \v 4 Nthhawi yabili anali kunkhala wovaliliwa ndi womangiwa ndi maceni. Anali kujuba ma cheni. panalibe amene anali ndi mpamvu zomugwila.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 5 Usiku ndi mzuba anali kukala ku manda ndi kumaphiri, analikulila ndi kuzicekha yeka ndi miyala yakutwa.
|
||||
\v 6 Pamene anaona Yesu kucokela patali, anatamangila kwa iye ndi kugwada ppkwa iye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 7 Analira kwambiri nati, "kodi takucimwirani ciyani, Yesu, mwana wa Mlungu wamwamba? Nikupempani mwa Mlungu kuti musaniceneke." \v 8 Cifukwa anali kunena kwa iye,"Tuluka mwa munthu uyu, iwe mizimu yonyansa."
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 9 Ndipo anamufunsa iye, "Zinalako ndiwe ndani? Ndipo anamuyankha nati, "Zina langa ndine Cigulu, cifukwa ndise ambiri."
|
||||
\v 10 Anamupempa iye mobwezela-bwezela kuti asavicose mumuzinda.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 11 Manje nkhumba zambiri zinali kudya pakaluphiri, \v 12 ndipo vinamupempha iye, kuti, "Titumene ku nkhumba; kuti tilowemo." \v 13 Ndipo anavilola; Mizimu yonyansa inacokandikungena mu nkhumba,ndipo zinautukila kuluphiri yopolika kucimana, ndipo nkhumba zokwanila tuwu sauzande zinambila mucimana.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 14 Ndipo aja wodyesa nkhumba zinja zinathaba anayenda ndi kuuza zamene zinacitika kumuzinda ndi malo wozungulila. Ndipo anthu ambiri anayenda kukaonelela zamene zinacitika.
|
||||
\v 15 Pamene anafika kwamene kunali Yesu anaona uja mwamuna uja amene anali ndi ziwanda- cikamu ca viwanda - alikhale pansi, atavala, ndipo ali ndi kuganiza bwino, ndipo anacita mantha.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 16 Aja amene anaona zamene zinacitika kuli uja mwamuna amene anali ndi ziwanda anawauza zamene zinacitika kuli iye ndi vyamene vinacitika ku nkhumba.
|
||||
\v 17 Ndipo anamupempha kuti acoke kumalo aja.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 18 Ndipo pamene anangena mu boti, uja mwamuna amene ziwanda zinacoka mwa iyeanapempha kuti ayende naye.
|
||||
\v 19 Koma iye anamukanila, koma iye anati, "Pita kunyumba yako ndi kuanthu ako kawauze zamene Ambuye akucitila iwe, ndicifundo camene akucitila iwe." \v 20 Iye anapita ndikuyamba kulankhula zinthu zikulu-zikulu zamene Yesu anamucitila iye ku Dekapolisi, ndipo wonse anadabwa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 21 Ndipo pamene Yesu anathauka kusidya ina, muboti, anthu ambiri anafika pamene anali iye, pamene anali mumbali mwa cimana. \v 22 Umodzi wa atsogoleli wa kacisi, woyitiwa Jailosi, anaza kwa iye pamene anamuona, anagwela pamendo pake. \v 23 Anamupemphatso ndi mobwezela, nati, "Mwana wanga mkazi alipafupi kufa. Ndikupemphani, kuti mubwele, kuti muzemumusanjike manja anu, kuti apole kuti ankhale ndi moyo." \v 24 Anayenda naye, ndipo anthu ambiri anamusatila iye ndikumukuza kwambiri.
|
|
@ -0,0 +1,3 @@
|
|||
\v 25 Apo panali mzimai amene anali wocoka magazi kwa zaka twelufu (12).
|
||||
\v 26 Anavutika kwambiri popita kuvipatala vyosiyana-siyana ndi anasewenzesa ndalama zake zonse, koma sanapole koma matenda anayendelela patsogolo.
|
||||
\v 27 Pamene anava zimene anthu analikulankula za Yesu, Iye anabwela ku mbuyo kwake pamene anali kuyenda, anagwila nsoga ya covala cake.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 28 Cifukwa anati, "Ngati ndingagwileko cabe covala cake, ndizacilisika." \v 29 Pamene anamugwila iye, magazi analeka kucoka, ndipo anamvela mutupi mwake kuti acilisika kumatenda aja.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 30 Panthawi yamene ijaYesu anazindikila kuti mpamvu zacoka muli iye. Ndipo anayangana kumbuyo kwamene kunali anthu ambiri nafunsa nati, "Ndani wanikuza covala canga?" \v 31 Wophunzila ake anati, "Muona anthu awa ambiri alikukugundani, ndipo inu mulikunena kuti, 'ndani wakugwilani?"' \v 32 Koma Yesu anayangana kuti amuone wamene anacita izi.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 33 Pamene mzimai, anaona zimene zinamucitikila, anacita mantha ndikuthutuma. Anabwela ndikugwa pansi pafupi ndi iye ndikumuuza coonadi conse pazimene zinacitika. \v 34 Anati kwa iye, "Mwana wanga mkazi, cikhulupiliro cako cakucilitsa. Pita mumtendele ndipo cilisika ku matenda yako."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 35 Pamene anali kulankhula naye, anthu ena anabwela kucokela kunyumba ya uja mtsogoleli wa sunagogi, nati, "mwana wanu mkazi wamwalila. Cifukwa ncani mupitiliza kumuvutisha mphunzitsi?"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 36 Koma pamene Yesu anamvako zimene analikulankhula, iye anati kumtsogoleli wa sunagogi, "Usacite mantha. Kuluphilira cabe." \v 37 Sanavomeze kuti wina ayende naye, koma Petulo, Yakobo ndi Yohana, ndimbale wa Yakobo. \v 38 Anafika kunyumba kwa uja mtsogoleli ndi anaona anthu ambiri alikumpanga congo; analikulira ndikupunda kwambiri.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 39 Pamene anangena munyumba, anati kwa iye, "Cifukwa nicani muli wosweka mitima ndipo muli kulira? uyu mwana sanafe wagona cabe." \v 40 Ndipo iwo anamuseka iye. Koma anawacosa panja ndipo anathenga atate ndi amake amwana ndi aja amene anabwela nawo, ndikupita mwamene munali mwana.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 41 Anathenga zanja la mwana ndipo anati, "Talitha Kumi,"kutanthauza kuti, "Mwana wacicepele, ndinena nawe, Uka." \v 42 Panthawi yamene ija mwana uja anauka ndikuyamba kuyenda (cifukwa anali twelufu (12) zaka) ndipo wonse anadabwa. \v 43 Ndipo anawauza mosimikiza kuti munthu aliyense asaziwe izi. ndipo anawauza kuti amupase mwana uja mkazi kuti ampase zakudya adye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 5
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 6 \v 1 Ndipo ancokako kuja ndi kupita kumuzida wake, ndipo wophunzira anamusata iye. \v 2 Pamene sabata inafika anali kuphunzitsa musunagoge. Anthu ambiri anamva ndipo anadabwisika. Anati, "Anacotsa kuti ziphunziso zotele?" "Kodi nzelu izi zamene zinapasidwa kwa iye nizabwanji?" "Nanga izi zodabwitsa zamene iye ali kucita?" \v 3 "Kodi uyu siuja mpala mathabwa mwana wa Maliya and mkwawo wa Yakobo na Joses na Yudas na Simoni? Nipo alongo ake sali naife pano?" Ndipo anakumudwisiwa ndi Yesu.
|
|
@ -0,0 +1,3 @@
|
|||
\v 4 Ndipo Yesu anati kwa iwo, "Mneneli samakhala opanda ulemo, kucosako cabe kumudzi kwake ndipakati ka enekwawo ndi banja yake."
|
||||
\v 5 Analepelakucita zambiri zodabwitsa, kucoselako cabe kusanjika manja yake paodwala ang'ono cabe ndikuwacilisa.
|
||||
\v 6 Kusakhulupirira kwawo kunamudabwisa iye. Ndipo anapita kumidzi yozungulira ndikuphunzitsa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 7 Ndipo anaitana aja twelufu (12) ndikuwatuma kuti apite awili - awili, ndipo anawapasa ulamuliro pamizimu yonyansa, \v 8 anawalamulira kuti asanyamule ciliconse paulendo, koma cabe ndodo: asanyamule buledi, kapena thumba, kapena ndalama mucikwama, \v 9 koma avale nkwabilo asavwale minjilo iwili.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 Ndipo anawauza kuti, " Pamene mungena munyumba, munkhale mwamene muja kufikila pamene muzacoka malo yaja. \v 11 Ndipo ngati mumzinda muja sanakulandileni kapena kukumvela inu, pamene mucoka malo aja mukunkhumule doti yakumendo kwanu ngati umboni kwa iwo."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Anapita kukalalikira kuti anthu atembenuke kucoka kuviipa vawo. \v 13 Anacosa ziwanda, ndi kuzoza ndi mafuta odwala ambiri ndipo anawacilitsa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 14 Mfumu Herode anavela izi, cifukwa zina la Yesu ianamveka pali ponse. Ena anati, "Yohane Mbatizi auka kwa kufa ndipo cifukwa ca ici, zodabwitsa za mpamvu zili kusewenza mwa iye." \v 15 Ndipo ena anati, " ndi Eliya." ena anatitso, "Ndi mneneli, ngati uja wa kale."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 16 Koma pamene Herode anamva izi anati, "Yohana wamene ndinadula mutu wauka." \v 17 Cifukwa Herode anatuma nthumi kuti Yohana amangiwe ndipo anamangiwa cifukwa ca Herodiya ( Mkazi wa mbale wakeFilipo) cifukwa anamkwatila iye.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 18 Cifukwa Yohana anamuuza Herode, " Sicinthuncovomelekeza kulti iwe umukwatile mkazi wa mbale wako." \v 19 Koma Herodiya iye anakwiya ndikufuna kumupa Yohana, koma analephela, \v 20 cifukwa Herode anaopa Yohana; anazindikila kuti anali wolunga ndipo woyela, ndipo anazimusunga bwino, kumvwelela iye kunamupanga iye kumvwela kuipa kwambiri, koma anamvwela mokondwela.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 21 Koma mpata unapezeka pamene Herode anali ndi pwando kusekelela siku yamene anabadwilamo ndipo anapanga cakudya camazulo ca anyanchito wake, ndi akulu asilikali ndi atsogoleli a Galileya.
|
||||
\v 22 Mwana mkazi wa Herodiya anaza kuzawabvinila, ndipo anakondwelesa Herode ndi alendo woitanidwa. Mfumu inati kukamsikana, "Nipemphe ciliconse camene ufuna nizakupasa."
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 23 Analapa kwa iye nati, " Ciliconse camene uzapempha kwa ine, nizakupasa, cukanga pakati ka ufumu wanga," \v 24 anabwelela kukafunsa amai ake, "Kodi ndikapemphe ciyani?" Anati, " Mutu wa Yohane mbatizi," \v 25 Ndipo anangena mwacangu panthawi yamene ija kwa mfumu, nati, " Ndifuna inu mundipase mwamsanga, pa mbale, mutu wa Yohana mbatizi."
|
|
@ -0,0 +1,3 @@
|
|||
\v 26 Ngakale kuti ici cinakumudwisa mfumu, sanakane kucitha cifukwa analonjeza kudala ndicikwa ca alendo aja amene anaitana.
|
||||
\v 27 Telo mfumu inatuma asilikali womuyanganila ndi akulu asilikakali kuti akamuletele mutu wa Yohana. Ndipo womuyanganila anayenda mundende ndikukajuwa mutu.
|
||||
\v 28 Anaubwelesa mutu pa mbale ndikuzapasa msikana ndi msikana anapasa amai ake. \v 29 Ndi wophunzila ake, pamene anamva izi, anabwela ndi kutenga mtembo ndikukaika ku m'manda.
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 30 Apositolo, anakumana pamodzi ndi Yesu, ndikumuuza iye zamane anacita ndi zamene anaphunzisa.
|
||||
\v 31 Ndipo iye anati kwa iwo,"Bwelani inu noka mupite kumalo kulibe anthu mukaphumuleko kwa kanthawi." Cifukwa ambiri anali kubwela ndikupita, analibe nthawi cukanga yakudya. \v 32 Ndipo anapita muboti kumalo yopanda anthu.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 33 Koma anawaonandipo ambiri anawazindikila iwo, ndipo anathawa ndi mendo m'muzinda wonse, ndipo anafika koyamba asanafike iwo. \v 34 Pamene anafika kumbali kwa cimana, anaona cigulu ca anthu ndipo anawacitila cifundo cifukwa anali ngati nkhosa yopanda mbusa. Anayamba kuwaphunzisa zinthu zambiri.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 35 Pamene nthawi inasila, wophunzila ake anaza kwaiye nati, "Aya malo niyopanda anthu ndipo nthawi yatha. \v 36 Muwalole awa anthu apite pafupi m'muzinda ndi m'minzi kuti akaguleko zakudya zawo."
|
|
@ -0,0 +1,2 @@
|
|||
\v 37 Koma iye anawayankha nati kwa iwo, "Imwe muwapase zakudya," Anati kuli iye, "Kodi tingayende kukagula ndi tuu hunderedi denari ya buledi ndi kuwapasa kuti adye?"
|
||||
\v 38 Iye anati kwa iwo,"Muli ndi buledi ingati? pitani mukaone." Pamene anaona anati, "Buledi mitanda isanu ndi nsomba ziwili."
|
Some files were not shown because too many files have changed in this diff Show More
Loading…
Reference in New Issue