nya-x-nyanja_mrk_text_reg/06/21.txt

2 lines
364 B
Plaintext
Raw Permalink Normal View History

\v 21 Koma mpata unapezeka pamene Herode anali ndi pwando kusekelela siku yamene anabadwilamo ndipo anapanga cakudya camazulo ca anyanchito wake, ndi akulu asilikali ndi atsogoleli a Galileya.
\v 22 Mwana mkazi wa Herodiya anaza kuzawabvinila, ndipo anakondwelesa Herode ndi alendo woitanidwa. Mfumu inati kukamsikana, "Nipemphe ciliconse camene ufuna nizakupasa."