Sat Oct 02 2021 09:42:52 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 09:42:53 +02:00
parent 15d5444847
commit f930554bd0
3 changed files with 5 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 29 \v 30 \v 31 Limeneli ndi lamulo lanu nthawi zonse kuti, m'mwezi wachisanu ndi chiwiri, pa tsiku lakhumi la mweziwo, mudzichepetse ndi kusagwira ntchito iliyonse, kaya ndi wobadwa kapena mlendo amene akukhala pakati panu. Izi zili choncho chifukwa tsiku lino lidzaphimbidwa machimo anu, kukuyeretsani ku machimo anu onse kuti mukhale oyera pamaso pa Yehova. Ili ndi Sabata lakupumula la inu, muyenera kudzichepetsa osagwira ntchito iliyonse. Limeneli ndi lamulo pakati panu nthawi zonse.
\v 29 Limeneli ndi lamulo lanu nthawi zonse kuti, m'mwezi wachisanu ndi chiwiri, pa tsiku lakhumi la mweziwo, mudzichepetse ndi kusagwira ntchito iliyonse, kaya ndi wobadwa kapena mlendo amene akukhala pakati panu. \v 30 Izi zili choncho chifukwa tsiku lino lidzaphimbidwa machimo anu, kukuyeretsani ku machimo anu onse kuti mukhale oyera pamaso pa Yehova. \v 31 Ili ndi Sabata lakupumula la inu, muyenera kudzichepetsa osagwira ntchito iliyonse. Limeneli ndi lamulo pakati panu nthawi zonse.

View File

@ -1 +1 @@
\v 32 \v 33 Mkulu wa ansembe, amene adzadzozedwe ndi kudzozedwa kuti akhale wansembe wamkulu m'malo mwa abambo ake, ayenera kupanga chotetezerachi ndi kuvala zovala zansalu, ndiye zovala zopatulika. Aziphimba malo opatulika koposa; azichita chotetezera chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo aphimbe machimo a ansembe ndi anthu onse a mumsonkhano.
\v 32 Mkulu wa ansembe, amene adzadzozedwe ndi kudzozedwa kuti akhale wansembe wamkulu m'malo mwa abambo ake, \v 33 ayenera kupanga chotetezerachi ndi kuvala zovala zansalu, ndiye zovala zopatulika. Aziphimba malo opatulika koposa; azichita chotetezera chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo aphimbe machimo a ansembe ndi anthu onse a mumsonkhano.

View File

@ -264,6 +264,9 @@
"16-23",
"16-25",
"16-27",
"16-29",
"16-32",
"16-34",
"17-title",
"17-01",
"17-05",