Sat Oct 02 2021 09:41:23 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 09:41:24 +02:00
parent 7c90287068
commit 15d5444847
3 changed files with 4 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 18 \v 20 \v 21 Munthu aliyense amene ali ndi chilema asayandikire kwa Yehova, monga munthu wakhungu kapena munthu amene satha kuyenda, wolumala kapena wolumala, \v 19 munthu amene ali ndi dzanja lopunduka kapena phazi, nsana kapena wochepa thupi kapena wamfupi modabwitsa, kapena mwamuna wopunduka m'maso mwake, kapena wodwala matenda, zilonda, nkhanambo, kapena amene machende ake aphwanyidwa. Munthu aliyense mwa ana a Aroni wansembe wopanda chilema asayandikire kukapereka nsembe zotentha ndi moto za Yehova. Munthu wotero ali ndi chilema; asayandikire kuti apereke chakudya cha Mulungu wake.
\v 18 Munthu aliyense amene ali ndi chilema asayandikire kwa Yehova, monga munthu wakhungu kapena munthu amene satha kuyenda, wolumala kapena wolumala, \v 19 munthu amene ali ndi dzanja lopunduka kapena phazi, \v 20 nsana kapena wochepa thupi kapena wamfupi modabwitsa, kapena mwamuna wopunduka m'maso mwake, kapena wodwala matenda, zilonda, nkhanambo, kapena amene machende ake aphwanyidwa. \v 21 Munthu aliyense mwa ana a Aroni wansembe wopanda chilema asayandikire kukapereka nsembe zotentha ndi moto za Yehova. Munthu wotero ali ndi chilema; asayandikire kuti apereke chakudya cha Mulungu wake.

View File

@ -1 +1 @@
\v 22 \v 23 \v 24 Akadye chakudya cha Mulungu wake, kaya ndi zopatulika koposa kapena zina zopatulika. Asalowe mkatikati mwa katani kapena kubwera pafupi ndi guwa lansembe, chifukwa ali ndi chilema, kuti angaipitse malo anga opatulika, chifukwa ine ndine Yehova amene ndimawapatula. '”Pamenepo Mose analankhula mawu amenewa. Aroni, ana ake, ndi anthu onse a Israeli.
\v 22 Akadye chakudya cha Mulungu wake, kaya ndi zopatulika koposa kapena zina zopatulika. \v 23 Asalowe mkatikati mwa katani kapena kubwera pafupi ndi guwa lansembe, chifukwa ali ndi chilema, kuti angaipitse malo anga opatulika, chifukwa ine ndine Yehova amene ndimawapatula. \v 24 '”Pamenepo Mose analankhula mawu amenewa. Aroni, ana ake, ndi anthu onse a Israeli.

View File

@ -325,6 +325,8 @@
"21-10",
"21-13",
"21-16",
"21-18",
"21-22",
"22-title",
"22-01",
"22-04",