Sun Oct 03 2021 17:25:57 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 17:25:58 +02:00
parent ad170e226f
commit 9b550dc6a7
5 changed files with 9 additions and 5 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 29 \v 30 Akangokhala chete, ndani angamuweruze? Ngati abisa nkhope yake, ndani angamuzindikire? Iye amalamulira pa dziko ndi anthu ena, kuti munthu wosapembedza asalamulire, kuti pasakhale wina wokopa anthu.
\v 29 Akangokhala chete, ndani angamuweruze? Ngati abisa nkhope yake, ndani angamuzindikire? Iye amalamulira pa dziko ndi anthu ena, \v 30 kuti munthu wosapembedza asalamulire, kuti pasakhale wina wokopa anthu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 32 \v 33 Munthu wina akauza Mulungu kuti, 'Ine ndachimwa, koma sindichimwanso; ndiphunzitseni zomwe sindingathe kuziona; Ndachita tchimo, koma sindidzachitanso. ' Kodi mukuganiza kuti Mulungu adzalanga tchimo la munthu ameneyo, popeza simukukonda zomwe Mulungu amachita? Muyenera kusankha, osati ine. Chifukwa chake nenani zomwe mukudziwa.
\v 31 Munthu wina akauza Mulungu kuti, 'Ine ndachimwa, koma sindichimwanso; \v 32 ndiphunzitseni zomwe sindingathe kuziona; Ndachita tchimo, koma sindidzachitanso. ' \v 33 Kodi mukuganiza kuti Mulungu adzalanga tchimo la munthu ameneyo, popeza simukukonda zomwe Mulungu amachita? Muyenera kusankha, osati ine. Chifukwa chake nenani zomwe mukudziwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 34 \v 35 Anthu anzeru adzanena ndi ine, inde, yense wanzeru wondimva Ine adzati, Yobu alankhula osadziwa; Mawu ake alibe nzeru. '
\v 34 Anthu anzeru adzanena ndi ine, inde, yense wanzeru wondimva Ine adzati, \v 35 Yobu alankhula osadziwa; Mawu ake alibe nzeru. '

View File

@ -1 +1 @@
\v 36 \v 37 Zikanakhala kuti Yobu anaimbidwa mlandu ngakhale pa nkhani zazingono za mlandu wake chifukwa cholankhula ngati anthu oipa. Pakuti akuwonjezera kupanduka pa tchimo lake; akuwomba m'manja potonza pakati pathu; Akuunjika mawu otsutsana ndi Mulungu. "
\v 36 Zikanakhala kuti Yobu anaimbidwa mlandu ngakhale pa nkhani zazingono za mlandu wake chifukwa cholankhula ngati anthu oipa. \v 37 Pakuti akuwonjezera kupanduka pa tchimo lake; akuwomba m'manja potonza pakati pathu; Akuunjika mawu otsutsana ndi Mulungu. "

View File

@ -413,6 +413,10 @@
"34-18",
"34-21",
"34-24",
"34-26"
"34-26",
"34-29",
"34-31",
"34-34",
"34-36"
]
}