Sun Oct 03 2021 17:24:43 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 17:24:43 +02:00
parent 495aa60af2
commit ad170e226f
7 changed files with 13 additions and 7 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 \v 15 Ndani anamuika woyang'anira dziko lapansi? Ndani adaika dziko lonse pansi pake? Ngati angakhazikitse zolinga zake pa iye yekha, ndipo ngati angabwezeretse kwa iye mzimu wake ndi mpweya wake, pamenepo anthu onse adzawonongeka pamodzi; anthu adzabwerera kufumbi.
\v 13 Ndani anamuika woyang'anira dziko lapansi? Ndani adaika dziko lonse pansi pake? \v 14 Ngati angakhazikitse zolinga zake pa iye yekha, ndipo ngati angabwezeretse kwa iye mzimu wake ndi mpweya wake, \v 15 pamenepo anthu onse adzawonongeka pamodzi; anthu adzabwerera kufumbi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 Ngati tsopano muli ndi chidziwitso, mverani ichi; mverani mawu anga. Kodi amene amadana ndi chilungamo angalamulire? Kodi muweruza Mulungu, wolungama ndi wamphamvu?
\v 16 Ngati tsopano muli ndi chidziwitso, mverani ichi; mverani mawu anga. \v 17 Kodi amene amadana ndi chilungamo angalamulire? Kodi muweruza Mulungu, wolungama ndi wamphamvu?

View File

@ -1 +1 @@
\v 18 \v 19 \v 20 Mulungu amene amati kwa mfumu, 'Inu ndinu oipa,' kapena amene munena kwa anthu olemekezeka kuti, 'Ndinu oipa'? Mulungu, amene samakondera atsogoleri ndipo salemekeza anthu olemera kuposa osauka, chifukwa onse ndi ntchito ya manja ake. Adzafa m'kamphindi, pakati pausiku anthu adzagwedezeka, nachoka; anthu amphamvu adzatengedwa, koma osati ndi manja a munthu.
\v 18 Mulungu amene amati kwa mfumu, 'Inu ndinu oipa,' kapena amene munena kwa anthu olemekezeka kuti, 'Ndinu oipa'? \v 19 Mulungu, amene samakondera atsogoleri ndipo salemekeza anthu olemera kuposa osauka, chifukwa onse ndi ntchito ya manja ake. \v 20 Adzafa m'kamphindi, pakati pausiku anthu adzagwedezeka, nachoka; anthu amphamvu adzatengedwa, koma osati ndi manja a munthu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 21 \v 22 \v 23 Pakuti maso a Mulungu amayang'ana njira za munthu; amapenya mayendedwe ake onse. Palibe mdima, kapena mdima wandiweyani kumene ochita zosalungama angabisalire. Pakuti Mulungu safunikiranso kusanthula munthu; palibe chifukwa choti munthu aliyense apite kukamuweruza.
\v 21 Pakuti maso a Mulungu amayang'ana njira za munthu; amapenya mayendedwe ake onse. \v 22 Palibe mdima, kapena mdima wandiweyani kumene ochita zosalungama angabisalire. \v 23 Pakuti Mulungu safunikiranso kusanthula munthu; palibe chifukwa choti munthu aliyense apite kukamuweruza.

View File

@ -1 +1 @@
\v 24 \v 25 Amaphwanyaphwanya amuna amphamvu chifukwa cha njira zawo zosafunikira kufufuzidwa; amaika ena m'malo awo. Mwa ichi akudziwa zochita zawo; agwetsa anthuwa usiku; awonongedwa.
\v 24 Amaphwanyaphwanya amuna amphamvu chifukwa cha njira zawo zosafunikira kufufuzidwa; amaika ena m'malo awo. \v 25 Mwa ichi akudziwa zochita zawo; agwetsa anthuwa usiku; awonongedwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 26 \v 27 \v 28 Poyera ena, amawapha chifukwa cha zoyipa zawo ngati zigawenga chifukwa adasiya kumutsata ndikukana kuvomereza njira zake zonse. Mwanjira iyi, adafuulira kulira kwa anthu osauka kudza kwa iye; anamva kulira kwa anthu ovutika.
\v 26 Poyera ena, amawapha chifukwa cha zoyipa zawo ngati zigawenga \v 27 chifukwa adasiya kumutsata ndikukana kuvomereza njira zake zonse. \v 28 Mwanjira iyi, adafuulira kulira kwa anthu osauka kudza kwa iye; anamva kulira kwa anthu ovutika.

View File

@ -407,6 +407,12 @@
"34-01",
"34-04",
"34-07",
"34-10"
"34-10",
"34-13",
"34-16",
"34-18",
"34-21",
"34-24",
"34-26"
]
}