Sun Oct 03 2021 16:37:02 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 16:37:03 +02:00
parent a1243a4ad8
commit 98dc3c38da
5 changed files with 7 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 11 \v 1 \v 2 \v 3 Kenako Zofari wa ku Naama anayankha kuti, "Kodi sayenera kuyankha mawu ochuluka chonchi? Kodi akuyenera kukhulupirira munthu ameneyu, wokonda kulankhula kwambiri? Kodi kudzitamandira kwanu kuyenera kuchititsa ena kukhala chete? Mukamanyoza, kodi palibe amene adzakupangitsani kuchita manyazi?
\c 11 \v 1 Kenako Zofari wa ku Naama anayankha kuti, \v 2 "Kodi sayenera kuyankha mawu ochuluka chonchi? Kodi akuyenera kukhulupirira munthu ameneyu, wokonda kulankhula kwambiri? \v 3 Kodi kudzitamandira kwanu kuyenera kuchititsa ena kukhala chete? Mukamanyoza, kodi palibe amene adzakupangitsani kuchita manyazi?

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 Iwe umati kwa Mulungu, 'Zikhulupiriro zanga ndi zoyera, ndipo ndimakhala wopanda cholakwa pamaso panu.' Koma, o, Mulungu akanati alankhule ndi kukutsegulirani milomo yake; 6kuti akakuwonetse zinsinsi za nzeru! Pakuti iye ndi wozindikira kwambiri. Dziwani tsono kuti Mulungu amafuna kwa inu zochepa zopyola muyeso wanu.
\v 4 Iwe umati kwa Mulungu, 'Zikhulupiriro zanga ndi zoyera, ndipo ndimakhala wopanda cholakwa pamaso panu.' \v 5 Koma, o, Mulungu akanati alankhule ndi kukutsegulirani milomo yake; \v 6 kuti akakuwonetse zinsinsi za nzeru! Pakuti iye ndi wozindikira kwambiri. Dziwani tsono kuti Mulungu amafuna kwa inu zochepa zopyola muyeso wanu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 \v 9 Kodi mungathe kumvetsetsa Mulungu pomufufuza? Kodi ukhoza kumvetsa Wamphamvuyonse mwangwiro? Nkhaniyi ndi yayitali kwambiri ngati kumwamba; mungatani? Ndizakuya kuposa kumanda; mungadziwe chiyani? Muyeso wake ndi wautali kuposa dziko lapansi, ndi wotambalala kuposa nyanja.
\v 7 \v 9 Kodi mungathe kumvetsetsa Mulungu pomufufuza? Kodi ukhoza kumvetsa Wamphamvuyonse mwangwiro? \v 8 Nkhaniyi ndi yayitali kwambiri ngati kumwamba; mungatani? Ndizakuya kuposa kumanda; mungadziwe chiyani? Muyeso wake ndi wautali kuposa dziko lapansi, ndi wotambalala kuposa nyanja.

1
11/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 11

View File

@ -145,6 +145,9 @@
"10-17",
"10-18",
"10-20",
"11-title",
"11-01",
"11-04",
"14-07",
"14-10",
"14-13",