Sun Oct 03 2021 16:34:17 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 16:34:17 +02:00
parent bd0c161d68
commit a1243a4ad8
5 changed files with 7 additions and 4 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 23 \v 24 \v 25 Akadzakhuta mimba yake, Mulungu adzaponyera pa iye ukali waukali wake; Mulungu adzavumbitsira mvula pa iye pamene iye akudya. Ngakhale munthu ameneyo adzathawa chida chachitsulo, uta wamkuwa udzawombera iye. Amachikoka kumsana kwake ndipo kuwala kwake kumatuluka pachiwindi. Ziwopsezo zimubwera.
\v 23 Akadzakhuta mimba yake, Mulungu adzaponyera pa iye ukali waukali wake; Mulungu adzavumbitsira mvula pa iye pamene iye akudya. \v 24 Ngakhale munthu ameneyo adzathawa chida chachitsulo, uta wamkuwa udzawombera iye. \v 25 Amachikoka kumsana kwake ndipo kuwala kwake kumatuluka pachiwindi. Ziwopsezo zimubwera.

View File

@ -1 +1 @@
\v 26 \v 27 Mdima wathunthu wasungira chuma chake. moto wosayatsidwa udza umeze; lidzadya chomwe chatsala m'hema wake. Kumwamba kudzaulula kusaweruzika kwake, ndipo dziko lapansi lidzamuukira ngati mboni.
\v 26 Mdima wathunthu wasungira chuma chake. moto wosayatsidwa udza umeze; lidzadya chomwe chatsala m'hema wake. \v 27 Kumwamba kudzaulula kusaweruzika kwake, ndipo dziko lapansi lidzamuukira ngati mboni.

View File

@ -1 +1 @@
\v 28 \v 29 Chuma cha m'nyumba yake chidzatha; katundu wake adzachoka tsiku la mkwiyo wa Mulungu. Ili ndilo gawo la munthu woyipa lochokera kwa Mulungu, Cholowa chosungidwa ndi Mulungu."
\v 28 Chuma cha m'nyumba yake chidzatha; katundu wake adzachoka tsiku la mkwiyo wa Mulungu. \v 29 Ili ndilo gawo la munthu woyipa lochokera kwa Mulungu, Cholowa chosungidwa ndi Mulungu."

View File

@ -1 +1 @@
MUTU 21
Mutu 21

View File

@ -218,6 +218,9 @@
"20-15",
"20-17",
"20-20",
"20-23",
"20-26",
"20-28",
"21-title",
"21-01",
"21-04",