Thu Oct 07 2021 14:35:08 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:35:09 +02:00
parent a8b38da7b1
commit 3e72f0f539
7 changed files with 12 additions and 6 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 32 Amapukusa phompho ngati thovu lamadzi otentha; amasandutsa nyanja ngati mphika wa mafuta. Akugalamuka kumbuyo kwake. wina angaganize kuti lakuya linali ndi imvi.
\v 31 Amapukusa phompho ngati thovu lamadzi otentha; amasandutsa nyanja ngati mphika wa mafuta. \v 32 Akugalamuka kumbuyo kwake. wina angaganize kuti lakuya linali ndi imvi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 33 \v 34 Padziko lapansi palibe wofanana naye, amene adapangidwa kukhala ndi moyo wopanda mantha. Amaona chilichonse chonyada; ndi mfumu ya ana onse onyada. "
\v 33 Padziko lapansi palibe wofanana naye, amene adapangidwa kukhala ndi moyo wopanda mantha. \v 34 Amaona chilichonse chonyada; ndi mfumu ya ana onse onyada. "

View File

@ -1 +1 @@
\c 42 \v 1 \v 2 \v 3 Ndipo Yobu anayankha Yehova, nati, Ndidziwa kuti inu mukhoza kuchita zonse, kuti palibe kanthu kadzakwaniritsidwa ndi inu. Zowonadi, ndalankhula zinthu zomwe sindimazimvetsa, zinthu zovuta kundimvetsa, zomwe sindimadziwa.
\c 42 \v 1 Ndipo Yobu anayankha Yehova, nati, \v 2 Ndidziwa kuti inu mukhoza kuchita zonse, kuti palibe kanthu kadzakwaniritsidwa ndi inu. \v 3 Zowonadi, ndalankhula zinthu zomwe sindimazimvetsa, zinthu zovuta kundimvetsa, zomwe sindimadziwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 Inu munandiuza kuti, 'Tamvera tsopano, ndiyankhula. Ndikufunsa zinthu, ndipo udzandiuza. ' Ndinali ndikumva za inu mwa khutu langa, koma tsopano diso langa lakuonani. Kotero ndimadzipeputsa ndekha; Ndikulapa m'fumbi ndi mapulusa. "
\v 4 Inu munandiuza kuti, 'Tamvera tsopano, ndiyankhula. \v 5 Ndikufunsa zinthu, ndipo udzandiuza. ' Ndinali ndikumva za inu mwa khutu langa, koma tsopano diso langa lakuonani. \v 6 Kotero ndimadzipeputsa ndekha; Ndikulapa m'fumbi ndi mapulusa. "

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 \v 9 Ndipo panali, atatha kunena ndi Yobu izi, Yehova anati kwa Elifazi wa ku Temani, Mkwiyo wanga wakuyakira iwe ndi mabwenzi ako awiri, chifukwa simunandinenera choyenera, monga anachitira Yobu mtumiki wanga. Tsopano tengani ng'ombe zamphongo zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri, pitani kwa mtumiki wanga Yobu, mudziperekere nsembe yopsereza: Mtumiki wanga Yobu adzakupemphererani, ndipo ndidzavomereza pemphero lake, kuti ndithane naye wakutsata pambuyo pa kupusa kwako, sunanene choyenera cha ine, monga anandichitira Yobu mtumiki wanga. " Pamenepo Elifazi wa ku Temani, Bilidadi wa ku Shuwa, ndi Zofari wa ku Naama ananka, nachita monga Yehova adawalamulira, ndipo Yehova anamlandira Yobu.
\v 7 Ndipo panali, atatha kunena ndi Yobu izi, Yehova anati kwa Elifazi wa ku Temani, Mkwiyo wanga wakuyakira iwe ndi mabwenzi ako awiri, chifukwa simunandinenera choyenera, monga anachitira Yobu mtumiki wanga. \v 8 Tsopano tengani ng'ombe zamphongo zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri, pitani kwa mtumiki wanga Yobu, mudziperekere nsembe yopsereza: Mtumiki wanga Yobu adzakupemphererani, ndipo ndidzavomereza pemphero lake, kuti ndithane naye wakutsata pambuyo pa kupusa kwako, sunanene choyenera cha ine, monga anandichitira Yobu mtumiki wanga. " \v 9 Pamenepo Elifazi wa ku Temani, Bilidadi wa ku Shuwa, ndi Zofari wa ku Naama ananka, nachita monga Yehova adawalamulira, ndipo Yehova anamlandira Yobu.

1
42/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 42

View File

@ -504,6 +504,11 @@
"41-19",
"41-22",
"41-25",
"41-28"
"41-28",
"41-31",
"41-33",
"42-title",
"42-01",
"42-04"
]
}