Thu Oct 07 2021 14:33:08 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:33:09 +02:00
parent 99b0e1e4ca
commit a8b38da7b1
7 changed files with 13 additions and 7 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 15 Ndani angavule chofunda chake? Ndani angalowe mkati mwa zida zake ziwiri? \v 14 Ndani angathe kutsegula zitseko za nkhope yake? nsana wake wapangidwa ndi mizere ya zikopa, zolimba pamodzi ngati ndi chidindo chomata.
\v 13 Ndani angavule chofunda chake? Ndani angalowe mkati mwa zida zake ziwiri? \v 14 Ndani angathe kutsegula zitseko za nkhope yake? \v 15 nsana wake wapangidwa ndi mizere ya zikopa, zolimba pamodzi ngati ndi chidindo chomata.

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 \v 18 Imodzi ili pafupi kwambiri ndi inzake kotero kuti mpweya sungalowe pakati pawo. Zalumikizana wina ndi mnzake; amamatira pamodzi, kotero kuti sangasunthidwe. Kuwala kukuwalira kuchokera mukufufuma kwake; maso ake ali ngati zikope za mbandakucha.
\v 16 Imodzi ili pafupi kwambiri ndi inzake kotero kuti mpweya sungalowe pakati pawo. \v 17 Zalumikizana wina ndi mnzake; amamatira pamodzi, kotero kuti sangasunthidwe. \v 18 Kuwala kukuwalira kuchokera mukufufuma kwake; maso ake ali ngati zikope za mbandakucha.

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 \v 20 \v 21 M'kamwa mwake mumatuluka muuni woyaka moto, ndi moto woyaka. M'mphuno mwake mumatuluka utsi ngati mphika wowira pamoto woyatsidwa kuti utenthe kwambiri. Mpweya wake uyatsa makala amoto; Moto umatuluka m'kamwa mwake.
\v 19 M'kamwa mwake mumatuluka muuni woyaka moto, ndi moto woyaka. \v 20 M'mphuno mwake mumatuluka utsi ngati mphika wowira pamoto woyatsidwa kuti utenthe kwambiri. \v 21 Mpweya wake uyatsa makala amoto; Moto umatuluka m'kamwa mwake.

View File

@ -1 +1 @@
\v 22 \v 23 \v 24 M'khosi mwake muli mphamvu, Ndipo zoopsa zimavina pamaso pake. Mapinda a thupi lake alumikizana; amukhazikika pa iye; sizingasunthike. Mtima wake ndi wolimba ngati mwala, inde, ndi wolimba ngati mphero yapansi.
\v 22 M'khosi mwake muli mphamvu, Ndipo zoopsa zimavina pamaso pake. \v 23 Mapinda a thupi lake alumikizana; amukhazikika pa iye; sizingasunthike. \v 24 Mtima wake ndi wolimba ngati mwala, inde, ndi wolimba ngati mphero yapansi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 25 \v 26 \v 27 Akadzuka, milungu imachita mantha; chifukwa cha mantha, akubwerera m'mbuyo. Lupanga likamugunda, silimachita kanthu, ngakhale mkondo, kapena muvi, kapena chida china chilichonse chosongoka. Amaganiza zachitsulo ngati udzu, ndi mkuwa ngati mtengo wowola.
\v 25 Akadzuka, milungu imachita mantha; chifukwa cha mantha, akubwerera m'mbuyo. \v 26 Lupanga likamugunda, silimachita kanthu, ngakhale mkondo, kapena muvi, kapena chida china chilichonse chosongoka. \v 27 Amaganiza zachitsulo ngati udzu, ndi mkuwa ngati mtengo wowola.

View File

@ -1 +1 @@
\v 28 \v 29 \v 30 Muvi sungampulumutse; kwa iye miyala ya gulaye ikhale mankhusu. Makalabu amaonedwa ngati udzu; akuseka kuwuluka kwa mkondo. Mbali zake zam'munsi zili ngati zidutswa zakuthwa; amasiya njira yotambalala m'matope ngati kuti akupunthira tirigu.
\v 28 Muvi sungampulumutse; kwa iye miyala ya gulaye ikhale mankhusu. \v 29 Makalabu amaonedwa ngati udzu; akuseka kuwuluka kwa mkondo. \v 30 Mbali zake zam'munsi zili ngati zidutswa zakuthwa; amasiya njira yotambalala m'matope ngati kuti akupunthira tirigu.

View File

@ -498,6 +498,12 @@
"41-01",
"41-04",
"41-07",
"41-10"
"41-10",
"41-13",
"41-16",
"41-19",
"41-22",
"41-25",
"41-28"
]
}