Fri Oct 01 2021 15:23:11 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
92cac92f80
commit
1f5f43c41a
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\c 3 \v 1 Taonani, Ambuye Yehova wa makamu atsala pang'ono kuchotsa ku Yerusalemu ndi ku Yuda thandizo ndi ndodo; chakudya chonse, ndi madzi onse, \v 2 munthu wamphamvu, wankhondo, woweruza, ndi mneneri, wakuchita kuwombeza ndi wamkulu, \v 3 mtsogoleri wa makumi asanu ndi nzika yolemekezeka, phungu, amisiri aluso, ndi wanyanga.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 4 "Ndidzaika achinyamata ngati atsogoleri awo, ndipo achinyamata adzawalamulira. \v 5 Anthu adzaponderezedwa wina ndi mnzake, ndipo aliyense ndi mnansi wake; mwanayo adzanyoza okalamba, ndipo onyozeka adzatsutsana ndi olemekezeka .
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 6 Mwamuna adzagwira m'bale wake m'nyumba ya bambo ake ndi kunena, 'Uli ndi malaya akunja; khala wolamulira wathu, ndipo kuwonongedwaku kukhale m'manja mwako. ' \v 7 Patsikulo adzafuula kuti, 'Sindikhala mchiritsi; Ndilibe mkate kapena chovala. Simundiyesa wolamulira anthu. '"
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mutu 3
|
|
@ -69,6 +69,10 @@
|
|||
"02-14",
|
||||
"02-17",
|
||||
"02-20",
|
||||
"03-title",
|
||||
"03-01",
|
||||
"03-04",
|
||||
"03-06",
|
||||
"04-01",
|
||||
"04-03",
|
||||
"04-05",
|
||||
|
|
Loading…
Reference in New Issue