Fri Oct 01 2021 15:21:11 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 15:21:12 +02:00
parent d6cec7fd96
commit 92cac92f80
4 changed files with 6 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 14 \v 15 \v 16 Tsiku la Yehova wa makamu lidzaukira mapiri onse ataliatali, ndi zitunda zonse zazitali, ndi nsanja zonse zazitali, ndi makoma onse osagwedezeka, ndi zombo zonse za Tarisi, ndi zombo zonse zokongola .
\v 14 Tsiku la Yehova wa makamu lidzaukira mapiri onse ataliatali, ndi zitunda zonse zazitali, \v 15 ndi nsanja zonse zazitali, ndi makoma onse osagwedezeka, \v 16 ndi zombo zonse za Tarisi, ndi zombo zonse zokongola .

1
02/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Kunyada kwa munthu kudzatsitsidwa, ndi kudzikuza kwa anthu kudzagwa; Yehova yekha adzakwezedwa tsiku lomwelo. \v 18 Mafano adzatha kwathunthu. \v 19 Amuna adzalowa m'mapanga a m'matanthwe ndi m'mapanga a nthaka chifukwa cha kuopsa kwa Yehova ndi ulemerero wa ukulu wake, pamene adzauka kuti aopsyeze dziko lapansi.

1
02/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Tsiku lomwelo anthu adzataya mafano awo a siliva ndi golidi omwe adadzipangira okha kuti azipembedza, ndipo adzawaponyera ku zipolowe ndi mileme. \v 21 Anthu adzalowa m'ming'alu ya m'matanthwe ndi m'ming'alu ya miyala yowopsya, chifukwa cha kuwopsa kwa Yehova ndi ulemerero wa ukulu wake, pamene adzauka kuti aopseze dziko lapansi. \v 22 Lekani kudalira munthu, yemwe mpweya wake wamoyo uli m'mphuno mwake, chifukwa amandiyendera chiyani?

View File

@ -66,6 +66,9 @@
"02-07",
"02-09",
"02-12",
"02-14",
"02-17",
"02-20",
"04-01",
"04-03",
"04-05",