Fri Nov 22 2019 17:52:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
805bfb1489
commit
82c0f56984
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 5 Bakapolo, muzinvelela ma bwana yanu akutupi na ulemu ukulu ndi kuyopa, ndi mutima wanu osakumbukira kanthu kena. \v 6 Banveleleni mwameni munganvelele Kristu. Musanvelele chabe pamene ma bwana yanu yakali kumiyangana, pakuti mubanvese mushe. Koma, munvelele monga bakapolo ba Kristu, bamene bachita chifunilo cha Mulungu kuchoka mu mutima wanu. \v 7 Sebenzani namitima zanu zonse, monga musebenzela Ambuye osati banthu, \v 8 chifukwa tiziba kuti chilichonse chabwino chamene wina achita, chizalandila chobwezela kwa Ambuye, angankale ni kapolo kapena omasuka.
|
Loading…
Reference in New Issue