Fri Nov 22 2019 17:50:44 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-11-22 17:50:44 +02:00
parent 838bf741f6
commit 805bfb1489
4 changed files with 4 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 32 \v 33 "Chifukwa chaichi mwamuna azasiya tate wake ndi mayi wake ndipo azapatikizana ku mukazi wake, ndipo aba babiri bazankala tupi imozi.” Ichi chonadi chobisika nichikulu koma nilikulankula pa nkani ya Kristu ndi mupingo. 33Komanso, aliyense pa inu afunika kukonda mukazi wake monga mwamene azikondela, na mukazi apase ulemu mwamuna wake.
\v 31 "Chifukwa chaichi mwamuna azasiya tate wake ndi mayi wake ndipo azapatikizana ku mukazi wake, ndipo aba babiri bazankala tupi imozi.” \v 32 Ichi chonadi chobisika nichikulu koma nilikulankula pa nkani ya Kristu ndi mupingo. \v 33 Komanso, aliyense pa inu afunika kukonda mukazi wake monga mwamene azikondela, na mukazi apase ulemu mwamuna wake.

1
06/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 6 \v 1 Bana, nvelelani makoro anu mwa Ambuye, chifukwa ichi nichabwino. \v 2 "Lemekeza tate wako ndi mayi” (ili ndiye lamulo loyamba lonkala nachilonjezano), \v 3 ”pakuti zinthu zizikuyendela mushe ndipo unkale ntawi ikulu pa ziko.”

1
06/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Atate, musakwiyise bana banu. Koma, mubakulise mukuzilesa na muchilangizo cha Ambuye.

1
06/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 6