Thu Apr 18 2024 12:06:21 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 12:06:21 +02:00
parent 8e497b425e
commit e77ec573f1
4 changed files with 3 additions and 1 deletions

1
17/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 17 \v 1 Yehosafati mwana wa Asa analowa ufumu mmalo mwake. Yehosafati anadzilimbitsa polimbana ndi Israyeli. \v 2 Anaika asilikali mmizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ya Yuda, nkuika asilikali ankhondo mdziko la Yuda ndi mmizinda ya Efuraimu imene Asa bambo ake anailanda.

1
17/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Yehova anali ndi Yehosafati chifukwa anayenda mnjira zoyambirira za Davide bambo ake, ndipo sanafunefune Abaala. [[V]] \v 4 Mmalo mwake, anadalira Mulungu wa bambo ake, ndipo anayenda mmalamulo ake, osati mogwirizana ndi zochita za Isiraeli.

1
17/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 17

View File

@ -182,7 +182,6 @@
"16-13",
"17-title",
"17-01",
"17-03",
"17-05",
"17-07",
"17-10",