Thu Apr 18 2024 11:56:19 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:56:19 +02:00
parent c47e6b0697
commit e58efe2460
3 changed files with 3 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 14 \v 15 Iwo analumbira kwa Yehova ndi mawu aakulu, ndi kufuula, ndi malipenga ndi malipenga. Ayuda onse anakondwera ndi lumbirolo, pakuti analumbira ndi mtima wawo wonse, ndipo anafunafuna Mulungu ndi chikhumbo chawo chonse, ndipo anampeza. Yehova anawapatsa mtendere wowazungulira.
\v 14 Iwo analumbira kwa Yehova ndi mawu aakulu, ndi kufuula, ndi malipenga ndi malipenga. \v 15 Ayuda onse anakondwera ndi lumbirolo, pakuti analumbira ndi mtima wawo wonse, ndipo anafunafuna Mulungu ndi chikhumbo chawo chonse, ndipo anampeza. Yehova anawapatsa mtendere wowazungulira.

1
15/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Mfumu Asa inachotsanso Maaka, agogo ake, pa udindo wake monga mayi wa mfumu, chifukwa anapanga fano lonyansa la mtengo wa Asera. Iye anadula chinthu chonyansacho, nkuchiphwanya mpaka kukhala fumbi, nkuchitentha pamtsinje wa Kidroni. \v 17 Koma misanje sinachotsedwa mu Isiraeli. Komabe, mtima wa Asa unali wodzipereka kwambiri masiku ake onse.

View File

@ -169,6 +169,7 @@
"15-08",
"15-10",
"15-12",
"15-14",
"15-16",
"15-18",
"16-title",