Thu Apr 18 2024 11:54:18 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:54:19 +02:00
parent ed5947e5cc
commit c47e6b0697
4 changed files with 4 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 \v 11 Choncho anasonkhana ku Yerusalemu mmwezi wachitatu, mchaka cha 15 cha ulamuliro wa Asa. Anaphera Yehova nsembe tsiku limenelo zina mwa zofunkha zimene anabwera nazo, ngombe mazana asanu ndi awiri, ndi nkhosa ndi mbuzi zikwi zisanu ndi ziwiri.
\v 10 Choncho anasonkhana ku Yerusalemu mmwezi wachitatu, mchaka cha 15 cha ulamuliro wa Asa. \v 11 Anaphera Yehova nsembe tsiku limenelo zina mwa zofunkha zimene anabwera nazo, ngombe mazana asanu ndi awiri, ndi nkhosa ndi mbuzi zikwi zisanu ndi ziwiri.

1
15/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Iwo anachita pangano kuti afunefune Yehova Mulungu wa makolo awo ndi mtima wawo wonse ndi moyo wawo wonse. \v 13 Iwo anagwirizana kuti aliyense amene akana kufunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli ayenera kuphedwa, kaya akhale wamngono kapena wamkulu, kaya akhale mwamuna kapena mkazi.

1
15/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 \v 15 Iwo analumbira kwa Yehova ndi mawu aakulu, ndi kufuula, ndi malipenga ndi malipenga. Ayuda onse anakondwera ndi lumbirolo, pakuti analumbira ndi mtima wawo wonse, ndipo anafunafuna Mulungu ndi chikhumbo chawo chonse, ndipo anampeza. Yehova anawapatsa mtendere wowazungulira.

View File

@ -167,8 +167,8 @@
"15-03",
"15-06",
"15-08",
"15-10",
"15-12",
"15-14",
"15-16",
"15-18",
"16-title",