Thu Apr 18 2024 11:38:18 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 11:38:19 +02:00
parent 2234b8b7ed
commit 466f3a519e
4 changed files with 4 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, + ndipo sitinamusiye. Tili ndi ansembe, zidzukulu za Aroni, otumikira Yehova, ndi Alevi amene amagwira ntchito yawo. Mmawa ndi madzulo onse amafukizira Yehova nsembe zopsereza ndi zofukiza zonunkhira bwino. + Iwo amakonzanso mkate woonekera patebulo loyera. azisamaliranso choikapo nyale chagolide, ndi nyali zake, aziyaka madzulo onse. Timasunga malamulo a Yehova Mulungu wathu, koma inu mwamusiya.
\v 10 Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, + ndipo sitinamusiye. Tili ndi ansembe, zidzukulu za Aroni, otumikira Yehova, ndi Alevi amene amagwira ntchito yawo. \v 11 Mmawa ndi madzulo onse amafukizira Yehova nsembe zopsereza ndi zofukiza zonunkhira bwino. Iwo amakonzanso mkate woonekera patebulo loyera. azisamaliranso choikapo nyale chagolide, ndi nyali zake, aziyaka madzulo onse. Timasunga malamulo a Yehova Mulungu wathu, koma inu mwamusiya.

1
13/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Taonani, Mulungu ali nafe kutitsogolera, ndipo ansembe ake ali pano ali ndi malipenga kuti akuliritseni. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu, pakuti simudzapambana.”

1
13/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Koma Yerobiamu anakonzera olalira pambuyo pao; ankhondo ake anali patsogolo pa Yuda, ndipo obisalirawo anali pambuyo pawo. \v 14 Pamene Yuda anacheuka, taonani, nkhondo inali patsogolo pao ndi pambuyo. Iwo anafuulira Yehova, ndipo ansembe analiza malipenga. \v 15 Pamenepo amuna a Yuda anapfuula; pamene anali kufuulira, Yehova anakantha Yerobiamu ndi Aisrayeli onse pamaso pa Abiya ndi Yuda.

View File

@ -150,6 +150,7 @@
"13-04",
"13-06",
"13-08",
"13-10",
"13-12",
"13-13",
"13-16",