Thu Apr 18 2024 12:08:21 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 12:08:22 +02:00
parent e77ec573f1
commit 08265202db
4 changed files with 4 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 Yehova anali ndi Yehosafati chifukwa anayenda mnjira zoyambirira za Davide bambo ake, ndipo sanafunefune Abaala. [[V]] \v 4 Mmalo mwake, anadalira Mulungu wa bambo ake, ndipo anayenda mmalamulo ake, osati mogwirizana ndi zochita za Isiraeli.
\v 3 Yehova anali ndi Yehosafati chifukwa anayenda mnjira zoyambirira za Davide bambo ake, ndipo sanafunefune Abaala. [[Mabaibulo ena akale alibe "David" , choncho, matembenuzidwe ena amakono amasiya.]] \v 4 Mmalo mwake, anadalira Mulungu wa bambo ake, ndipo anayenda mmalamulo ake, osati mogwirizana ndi zochita za Isiraeli.

1
17/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Momwemo Yehova anakhazikitsa lamulo m'dzanja lace; Ayuda onse anabweretsa mitulo kwa Yehosafati. Anali ndi chuma ndi ulemu wochuluka. \v 6 Mtima wake unali wodzipereka ku njira za Yehova. + Anachotsanso misanje ndi mizati ya Asera mYuda.

1
17/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Mchaka chachitatu cha ulamuliro wake, anatumiza akalonga ake, Beni-Haili, Obadiya, Zekariya, Netaneli ndi Mikaya kuti akaphunzitse mmizinda ya Yuda. \v 8 pamodzi ndi Alevi: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya, ndi Tobi-Adoniya; ndi pamodzi nao panali Elisama ndi Yehoramu ansembe. \v 9 Anaphunzitsa mYuda, ali nalo buku la chilamulo cha Yehova; Iwo anayendayenda mmizinda yonse ya Yuda ndi kuphunzitsa pakati pa anthu.

View File

@ -182,8 +182,8 @@
"16-13",
"17-title",
"17-01",
"17-03",
"17-05",
"17-07",
"17-10",
"17-12",
"17-14",