nya-x-nyanja_1ki_text_reg/14/06.txt

1 line
528 B
Plaintext
Raw Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 6 Ahiya atamva kugunda kwa mapazi ake akulowa pakhomo, anati: “Lowa, mkazi wa Yerobiamu. Nchifukwa chiyani ukudziyerekezera kuti ndiwe munthu? \v 7 Ukauze Yerobiamu kuti, Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, Ndinakukweza pakati pa anthu kuti ndikuike kukhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli, \v 8 ndipo ndinangamba ufumuwo kuuchotsa pa banja la Davide ndi kuupereka kwa iwe monga Davide mtumiki wanga, amene anasunga malamulo anga, nanditsata ine ndi mtima wake wonse, kuchita yekha zoyenera pamaso panga.