nya-x-nyanja_1ki_text_reg/21/27.txt

1 line
436 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 27 Ahabu atamva mawu amenewa, anangamba zovala zake nkuvala chiguduli nkusala kudya, nkugona chiguduli ndi kumva chisoni kwambiri. \v 28 Pamenepo mawu a Yehova anafika kwa Eliya wa ku Tisibe, kuti: \v 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga? Popeza wadzichepetsa pamaso panga, sindidzabweretsa tsoka limene likubwera mmasiku ake, + chifukwa mtsiku la mwana wake ndidzabweretsa tsoka pa banja lake.