nya-x-nyanja_1ki_text_reg/14/23.txt

1 line
297 B
Plaintext
Raw Permalink Blame History

This file contains ambiguous Unicode characters

This file contains Unicode characters that might be confused with other characters. If you think that this is intentional, you can safely ignore this warning. Use the Escape button to reveal them.

\v 23 Iwo anadzimangiranso malo okwezeka, zipilala zamiyala ndi mizati ya Asera pa zitunda zonse zazitali ndi pansi pa mtengo uliwonse wa masamba obiriwira. \v 24 Mdzikomo munalinso mahule achipembedzo. Anachita zonyansa ngati zimene amitundu amene Yehova anawaingitsa pamaso pa ana a Isiraeli.